Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • es18 tsamba 6
  • Mmene Mungagwiritsire Ntchito Kabukuka

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Mmene Mungagwiritsire Ntchito Kabukuka
  • Kuphunzira Malemba Tsiku ndi Tsiku—2018
  • Timitu
Kuphunzira Malemba Tsiku ndi Tsiku—2018
es18 tsamba 6

Mmene Mungagwiritsire Ntchito Kabukuka

M’masamba otsatirawa muona kuti tsiku lililonse lili ndi lemba lake komanso ndemanga yake. Ngakhale kuti mukhoza kupanga lemba la tsiku nthawi ina iliyonse, ena amaona kuti zimakhala zothandiza kwambiri kupanga m’mawa. Zimenezi zimawathandiza kuti aziganizira mfundo za m’lembalo tsiku lonse. Kupanga lemba la tsiku ndi banja lanu n’kothandizanso kwambiri. Anthu otumikira pa Beteli padziko lonse amakambirana lemba la tsiku pa nthawi ya chakudya cham’mawa.

Ndemanga zomwe zili m’kabukuka zinatengedwa mu Nsanja ya Olonda (w) yophunzira kuyambira ya mwezi wa April 2016 mpaka March 2017. Manambala olembedwa kumapeto kwa deti la magazini a Nsanja ya Olonda, akusonyeza nambala ya nkhani yophunzira (1, 2, 3, 4 kapena 5) ya m’magaziniyo. Kenako pali nambala ya ndime imene ndemangayo yachokera. (Onani chitsanzo chili m’munsichi.) Komanso mungapeze mfundo zambiri mu nkhani imene mwachokera ndemangayo. Kuti mudziwe tsamba limene nkhani iliyonse yayambira, onani tsamba 2 mu Nsanja ya Olonda imene nkhaniyo yachokera.

[Chithunzi patsamba 6]

    Mabuku a Chichewa (1974-2026)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena