Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • scl tsamba 57
  • Kunama

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Kunama
  • Malemba Othandiza pa Moyo wa Chikhristu
Malemba Othandiza pa Moyo wa Chikhristu
scl tsamba 57

Kunama

Kodi Yehova amaona bwanji anthu omwe sasunga malonjezo awo?

Aro 1:31, 32

Onaninso Sl 15:4; Mt 5:37

  • Nkhani za m’Baibulo zomwe zingakuthandizeni:

    • Eks 9:27, 28, 34, 35​—Farao analola kuti anthu a Mulungu apite, koma kenako anasintha maganizo ake

    • Eze 17:11-15, 19, 20​—Yehova analanga Mfumu Zedekiya chifukwa chonyoza lumbiro lake ndiponso chifukwa chophwanya pangano lake ndi mfumu ya Babulo

    • Mac 5:1-10​—Hananiya, ndi mkazi wake Safira, ananama kuti apereka kumpingo ndalama zonse zimene anapeza atagulitsa munda wawo

Kodi Yehova amaona bwanji anthu amiseche?

Sl 15:1-3; Miy 6:16-19; 16:28; Akl 3:9

Onaninso Miy 11:13; 1Ti 3:11

  • Nkhani za m’Baibulo zomwe zingakuthandizeni:

    • 2Sa 16:1-4; 19:24-30​—Ziba ananena zinthu zabodza zokhudza mbuye wake wokhulupirika Mefiboseti

    • Chv 12:9, 10​—Mdyerekezi, kapena kuti Woneneza, amaneneza atumiki a Mulungu nthawi ndi nthawi

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena