Kudziletsa
Kodi Yehova amasonyeza bwanji kudziletsa?
Kodi ndi mbali ziti pa moyo wathu zomwe timafunika kudziletsa?
Miy 16:32; 25:28; 1Ak 9:25, 27
Onaninso 2Ti 2:23-25; Tit 1:7, 8
Nkhani za m’Baibulo zomwe zingakuthandizeni:
2Sa 16:5-14—Mfumu Davide anadziletsa pamene Simeyi anamulankhula mawu onyoza komanso kumuchitira zinthu mopanda ulemu
1Pe 2:21-23—Mtumwi Petulo anafotokoza kuti Yesu anasonyeza kuleza mtima kwambiri pamene anthu ankamuchitira zachipongwe komanso kumuzunza
N’chiyani chingatithandize kuti tipitirize kudziletsa?
Lu 11:9-13; Aga 5:22, 23; Aef 4:23, 24; Akl 4:2
Nkhani za m’Baibulo zomwe zingakuthandizeni:
Lu 11:5-8—Yesu anafotokoza kufunika kopitiriza kupempha kuti tithandizidwe