Kodi n’zotheka kukhala ndi moyo mpaka kalekale?
“Olungama adzalandira dziko lapansi, ndipo adzakhala mmenemo mpaka kalekale.”—Salimo 37:29.
Baibulo limanena kuti m’tsogolo
Aliyense adzakhala ndi thanzi labwino.—Yesaya 33:24; 35:5, 6.
Chilengedwe chidzabwereranso mwakale.—Yesaya 35:1, 2; Chivumbulutso 11:18.
Kuti mudziwe zambiri, pitani pa jw.org.
© 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania