Kodi pali amene amamvetsera mapemphero athu?
“Inu Wakumva pemphero, anthu a mitundu yonse adzabwera kwa inu.”—Salimo 65:2.
Baibulo limatiuza
Mmene tingapempherere.—Mateyu 6:7-13.
Kuti Mulungu amayankha mapemphero ochokera pansi pa mtima.—Mateyu 7:7, 8.
Kuti mudziwe zambiri, pitani pa jw.org.
© 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania