Kodi malangizo a Yesu ndi othandizabe masiku ano?
“Zonse zimene mukufuna kuti anthu akuchitireni, inunso muwachitire zomwezo.”—Mateyu 7:12.
Yesu anaphunzitsanso kuti
Tingachepetse nkhawa tikamapewa kudera nkhawa za mawa.—Mateyu 6:34.
Tizikhululukira ena.—Mateyu 6:14, 15.
Kuti mudziwe zambiri, pitani pa jw.org.
© 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania