Kodi Ufumu wa Mulungu udzathetsa bwanji mavuto athu?
“Oipa sadzakhalaponso . . . Ofatsa adzalandira dziko lapansi.”—Salimo 37:10, 11.
Baibulo limanena kuti Ufumu wa Mulungu
Ndi boma lenileni la kumwamba.—Danieli 2:44; 7:14.
Udzatipatsa zonse zimene timafunikira.—Yesaya 65:21-23.
Kuti mudziwe zambiri, pitani pa jw.org.
© 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania