Kodi zipembedzo zonse zimasangalatsa Mulungu?
“Geti lolowera ku moyo ndi lalingʼono komanso msewu wake ndi wopanikiza ndipo amene akuupeza ndi ochepa.”—Mateyu 7:14.
Baibulo limanena kuti
Si zipembedzo zonse zomwe zimasangalatsa Mulungu.—Mateyu 7:21-23; Maliko 7:6-8.
Akhristu oona amalimbikitsa mtendere komanso chikondi.—Mika 4:3; Yohane 13:35.
Kuti mudziwe zambiri, pitani pa jw.org.
© 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania