Mutu wa Buku Lino/Tsamba la Ofalitsa
Buku la Mboni za Yehova Lofufuzira Nkhani
la 2019
La Zinthu Zimene Zinatuluka M’Chichewa
“Yehova amapereka nzeru. Kudziwa zinthu ndi kuzindikira kumatuluka m’kamwa mwake.”—Miyambo 2:6.
Note: Some direction given in older referenced material is no longer current.
Bukuli sitigulitsa. Timalipereka ngati njira imodzi yophunzitsira anthu Baibulo padziko lonse ndipo ndalama zoyendetsera ntchitoyi ndi zimene anthu amapereka mwakufuna kwawo.
Ngati mukufuna kupereka pitani pa webusaiti yathu ya www.pr418.com.
Buku la Mboni za Yehova Lofufuzira Nkhani la 2019
La Zinthu Zimene Zinatuluka M’Chichewa
Losindikizidwa mu January 2024
Chichewa (rsg19-CN)
© 2020, 2022, 2024 WATCH TOWER BIBLE AND TRACT SOCIETY OF PENNSYLVANIA