Kodi Munaphonya Iwo?
◼ Kodi Akufa Ali ndi Moyo
◼ Kulimbanira Ulamuliro Wadziko Lonse—Kodi Adzapambana Ndani?
◼ Kodi Tiri “m’Nthawi Yamapeto”?
◼ AIDS—Kodi Ndani Amene Ali Pangozi?
Kodi Mungadzitetezere Motani?
◼ Uchigawenga—Kodi Aliyense Ngwotetezereka?
◼ Kumwa ndi Kuyendetsa Galimoto
Zapamwambazo ziri kokha mitu yochepa yokwaniritsidwa mu Nsanja ya Olonda ndi magazini inzake Galamukani! mkati mwa chaka chapita, ndipo zikuimira mtundu wa nkhani zokonzekeretsedwa kaamba ka inu miyezi irinkudza.
Kuchitira chitsanzo kufunika kwa Galamukani!, pamene mphunzitsi wa oyendetsa magalimoto anapeza kope ya “Kumwa ndi Kuyendetsa Galimoto,” iye anaorda makope oposa 400 kaamba ka kugwiritsira ntchito mu programu yawo yamaphunziro a oyendetsa magalimoto.
MUSAPHONYE MIYEZI 12 IRIKUDZAYO
Chonde tumizani kulembetsa kwa chaka chimodzi kwa Nsanja ya Olonda ndi Galamukani! ndatumiza K48. 00.