Pangani Kuŵerenga Baibulo Kukhala kwa Tanthauzo Mokulira
New World Translation of the Holy Scriptures—With References m’chenicheni imapanga chimenechi.
Woŵerenga woyamikira posachedwapa analemba ponena za New World Translation Reference Bible: “Liri yankho ku mapemphero anga. Pamene ndipanga kuŵerenga kwanga kwa Baibulo, ndimafufuza zambiri za zilozerozo. Zimandithandiza ine kuwona maprinsipulo ena ofunika kwambiri amene ali ogwirizana ndi nkhaniyo. Icho mowonadi chimafutukula kumvetsetsa kwanga, ndipo ndingapange kugwiritsira ntchito kwaumwini kwabwinopo.”
Chofalitsidwa cha wophunzira chimenechi chiri chokutidwa ndi chikuto cholimba cha dark-maroon ndipo chiri ndi mawu a m’munsi oposa 11,000, indekisi yaikulu yosonyeza mawu enieni m’lembalo, ndi mapu. Kokha K72.00.
Chonde tumizani, mutalipiriratu positi, New World Translation of the Holy Scriptures—With References. Ndatsekeramo K72.00. (Kunja kwa Zambia, lemberani nthambi ya Watch Tower ya kwanuko kaamba ka chidziŵitso.)