Kodi Mungakonde Kuchezeredwa?
Ngakhale m’dziko lino lodzala ndi mavuto mungakhoze kupeza chimwemwe kuchokera m’chidziwitso cholongosoka cha Baibulo chonena za Mulungu, Ufumu wake, ndi chifuno chake chabwino kwambiri kwa anthu. Ngati mungafune chidziwitso chowonjezereka kapena ngati mungakonde kuti wina adze kudzachita nanu phunziro Labaibulo lapanyumba laulere, chonde lemberani ku Watch Tower, Box 33459, Lusaka 10101, kapena ku keyala yoyenera pandandanda ya patsamba 2.