Zisonyezero za Nkhani za mu Nsanja ya Olonda za 1993
Zosonyezera deti la kope limene nkhaniyo ikupezeka
BAIBULO
Chitsogozo Chogwira Ntchito cha Munthu Wamakono, 5/1
Malo Otchulidwa m’Baibulo, 6/15
Maulosi a Baibulo, 5/15
Mbiri ya Baibulo, 6/1
Tifunikira Baibulo? 5/1
LIPOTI LA OLENGEZA UFUMU
2/1, 3/1, 5/1, 7/1, 8/1, 10/1, 11/1
MAFUNSO OCHOKERA KWA OŴERENGA
Akristu ndi kuipitsidwa kwa malo, 1/1
Kodi Paulo akapereka moyo wake kaamba ka Ayuda? (Aroma 9:3), 9/15
Kuchita bizinesi ndi wosakhulupirira? 10/1
Kulephera kufika pa Chikumbutso, 2/1
Matikiti a mwaŵi, 6/15
Melikizedeke “wopanda maŵerengedwe a chibadwidwe chake,” (Aheb. 7:3), 11/15
Osakhulupirira amene afa chisautso chachikulu chisanayambe, 5/15
“Wopatsidwa mphatso ya mzimu” (1 Akor. 14:37), 10/15
Wosakhoza kupeza mnzake wamuukwati, 1/15
MALO A KU DZIKO LOLONJEZEDWA
Beeriseba, 7/1
Gerizimu, 1/1
Gilieadi, 9/1
Kondwerani! Nsupa Zisefukira Ndi Mafuta, 3/1
Nyanja ya Galileya, 11/1
Sinai—Phiri la Mose ndi Chifundo, 5/1
MBONI ZA YEHOVA
Amishonale ku Micronesia, 3/1
Anamenyera Nkhondo Chikhulupiriro Chake (C. Bazán Listán), 6/15
Bwalo Lamilandu Lalikulu la Ulaya Lichilikiza Kuyenera kwa Kulalikira m’Greece, 9/1
Katundu Wachithandizo Asonyeza Chikondi Chachikristu (Russia, Ukraine), 2/1
Kulalikira Kumudzi ndi Mudzi ku Spain, 11/15
Kulalikira m’Dziko la Zinthu Zosiyanasiyana (Australia), 10/15
Kulalikira ndi Chipiriro m’Dziko la Madzi Oundana ndi la Moto (Iceland), 9/15
Kupeza Chuma Chenicheni mu Hong Kong, 5/15
Kutumba kwa Mtundu Wosiyana (Bahamas), 3/15
Limbikirani Muutumiki Waupainiya, 9/15
Maphunziro a Gileadi, 12/1
Misonkhano ya Chigawo ya “Chiphunzitso Chaumulungu,” 2/15
Misonkhano ya Chigawo ya “Onyamula Kuunika,” 1/15
Mulungu Samaiwala ‘Chikondi Chimene Munachiwonetsera’ (Eastern Europe), 1/1
“Olengeza Ufumu” Amaloŵa Pamadzi a Guyana, 4/1
Sukulu ya Gileadi—Ya Zaka 50 Ndipo Ikupitabe Patsogolo! 6/1
Yehova Asanduliza Nthaŵi ndi Nyengo mu Romania, 6/15
Yehova Atetezera Anthu Ake mu Hungary, 7/15
MOYO NDI MIKHALIDWE YACHIKRISTU
Akristu Ayenera Kusunga Tsiku Lakupuma? 2/15
Amaŵeta Nkhosa Mwachifundo, 9/15
Chifukwa Chake Mufunikira Kufika Pamisonkhano Yachikristu? 8/15
Chikondi cha pa Mnansi, 9/15
Chiyembekezo—Chinjirizo Lofunika, 4/15
“Funani Yehova, Ofatsa Inu Nonse,” 12/15
Khalani Achimwemwe ndi Adongosolo, 4/1
Kodi Mukuchita Zoposa? 4/15
Kodi Nkutumikiriranji Yehova? 5/15
Kodi Nkuvomereranji Cholakwa? 11/15
Kulankhulana—Kuposa Kukambitsirana Chabe, 8/1
Kuphunzira Kuyembekezera, 10/15
Kusamalira Okalamba, 2/15
Kusunga Diso Lathu Lili “la Kumodzi” m’Ntchito Yaufumu, 12/15
Kuweta Nkhosa za Mtengo Wake za Yehova Mokoma Mtima, 7/15
Lamulo la Mkhalidwe Kapena Kutchuka? 10/1
Lingaliro Loyenera la Chifundo cha Mulungu, 10/1
Mfungulo ya Moyo Wabanja Wachipambano, 10/1
Mmene Akristu Angathandizire Okalamba, 8/15
Mmene Mungalimbitsire Zomangira Zaukwati, 8/15
Mpatsi wa “Mphatso Iliyonse Yabwino,” 12/1
Mulungu Amakulitsa—Mumachita Mbali Yanu? 3/1
Mumalemekeza Malo Anu Olambirira? 6/15
Mumatsatira Yehova ndi Mtima Wonse? 5/15
Ulemerero wa Imvi, 3/15
Yehova Amakumbukira Odwala ndi Okalamba, 8/1
NKHANI ZA MOYO WA ANTHU
Choloŵa Chapadera Chachikristu (B. Brandt), 10/1
Kufupidwa ndi “Kolona wa Moyo” (F. Franz), 3/15
Kukula ndi Gulu la Yehova m’South Africa (F. Muller), 4/1
Kusindikiza Mabuku Ofotokoza Baibulo Mkati mwa Chiletso (M. Vale), 7/1
Kutumikira ndi Lingaliro la Kufulumira kwa Nthaŵi (H. van Vuure), 11/1
Kuyamikira Chichilikizo Chosalekeza cha Yehova (S. Gaskins), 6/1
Ndinapeza Chikhutiro Kutumikira Mulungu (J. Thongoana), 2/1
“Ndine Pano; Munditumize Ine” (W. John), 5/1
Yehova, Chidaliro Changa Kuyambira Paubwana Wanga (B. Tsatos), 8/1
Yehova Anandichirikiza m’Ndende ya m’Chipululu (I. Mnwe), 3/1
NKHANI ZAZIKULU ZOPHUNZIRIDWA
Achichepere—Kodi Mukulondola Chiyani? 4/15
Achimwemwe Ali Odzichepetsa, 12/1
Akristu ndi Chitaganya cha Anthu Lerolino, 7/1
Banja Lachikristu Limachitira Zinthu Pamodzi, 9/1
Banja Lachikristu Limaika Zinthu Zauzimu Poyamba, 9/1
Banja Lachikristu Limathandiza Okalamba, 9/1
Chenjerani ndi Nyimbo Zosayenera! 4/15
Chifundo cha Yehova Chimatipulumutsa Kukugwiritsidwa Mwala, 3/15
Chikondi (Agape)—Zimene Sichili ndi Zimene Chili, 10/15
Chilakiko Chotsiriza cha Mikaeli, Kalonga Wamkulu, 11/1
Chilanditso pa Vumbulutso la Yesu Kristu, 5/1
Chilengedwe Chimati ‘Sangaŵiringule,’ 6/15
Chipiriro—Nchofunika kwa Akristu, 9/15
Dalirani Yehova! 12/15
Dziŵani Yehova Kupyolera m’Mawu Ake, 6/15
‘Itanani Akulu,” 5/15
Khalani Olama m’Maganizo—Mapeto Ayandikira, 6/1
Khalani Olimba Mtima! 11/15
Khalani Osandulika m’Maganizo ndi Ounikiridwa Mumtima, 3/1
Kodi Mulungu Amakudziŵanidi? 10/1
Kodi Ndani Amene Akutsatira Kuunika kwa Dziko? 4/1
Kodi Nkupeŵeranji Kulambira Mafano? 1/15
Kodi Tingawonjezere Motani Ukoma Pachikhulupiriro Chathu? 7/15
Kugonjera Kwaumulungu—Chifukwa Ninji Ndipo ndi Yani? 2/1
Kukondwera mwa Mlengi Wathu Wamkulu, 1/1
Kukulitsa Mantha Aumulungu, 12/15
Kukulitsa Umunthu Watsopano mu Ukwati, 2/15
Kupeza Mfungulo ya Chikondi cha pa Abale, 10/15
Kutumikira Yehova ndi Mzimu Wodzimana, 6/1
Kuunikira Chidziŵitso pa Kukhalapo kwa Kristu, 5/1
Kuŵeta Limodzi ndi Mlengi Wathu Wamkulu, 1/1
Kuyenda Mwanzeru m’Dzikoli, 7/1
Labadirani Malonjezo a Mulungu mwa Kusonyeza Chikhulupiriro, 7/15
Lolani Kudziletsa Kwanu Kukhalepo Nikusefukire, 8/15
Masiku Aulosi a Danieli ndi Chikhulupiriro Chathu, 11/1
Mfumu Idetsa Malo Opatulika a Yehova, 11/1
“Mundisanthule, Mulungu”, 10/1
Musalole Aliyense Kukuipsirani Makhalidwe Anu Okoma, 8/1
Ntchito Zowonjezereka Mkati mwa Kukhalapo kwa Kristu, 5/1
Onyamula Kuunika—Kaamba ka Chifuno Chotani? 1/15
Pambanani m’Kupeŵa Msampha wa Kusirira, 8/1
Peŵani Kulambira Mafano Kwamtundu Uliwonse, 1/15
Pitirizani Kukula m’Chidziŵitso, 8/15
“Pitirizanibe Kuyenda Monga Ana a Kuunika,” 3/1
Tsatirani Kuunika kwa Dziko, 4/1
“Ukwati Ukhaletu Wolemekezeka Pakati pa Onse,” 2/15
Ŵetani Gulu la Nkhosa la Mulungu Mofunitsitsa, 5/15
Wonjezerani Pachipiriro Chanu Kudzipereka Kwaumulungu, 9/15
Yehova Samapeputsa Mtima Wosweka, 3/15
Yendani Molimba Mtima m’Njira za Yehova, 11/15
Zimene Kugonjera Kwaumulungu Kumafuna kwa Ife, 2/1
Zitsanzo za Kudzichepetsa Zoyenera Kutsanziridwa, 12/1
NKHANI ZOSIYANASIYANA
Akristu Oyambirira ndi Dziko, 7/1
Batizani! Batizani! Batizani!—Koma Chifukwa Ninji? 4/1
Chikondi cha pa Ndalama, 2/15
Fodya ndi Atsogoleri Achipembedzo, 2/1
Helo, 4/15
Kodi Chabwino Chidzagonjetsadi Choipa? 2/1
Kodi Kuba Kudzatha Konse? 10/15
Kodi Kuthiridwa Mwazi Kumathokozedwa Mopambanitsa? 10/15
Kodi Mudzakwatulidwira Kumwamba? 1/15
Kodi Mumafunikiranji Kuti Mukhale Wachimwemwe? 6/1
Kodi Mungakhale ndi Moyo Kwautali Wotani? 11/15
Kodi Muyenera Kubatizidwa? 4/1
Kulemera Kungayese Chikhulupiriro Chanu, 7/15
Kuyeretsa Kwapadziko, 2/15
Kuzengereza Nkwakupha! 3/1
Masoka Achilengedwe, 12/1
“Mdani Wotsiriza” Adzagonjetsedwa! 11/15
Mgonero wa Ambuye, 3/15
Mkhalidwe Wamoyo wa Wodandaula Suli Wachimwemwe, 3/15
Mmene Dziko Lachikristu Linakhalira Mbali ya Dziko, 7/1
Ndodo Yachifumu ya Makangaza, 4/15
Papias Anaona Mawu a Ambuye Kukhala Amtengo Wapatali, 9/15
Peŵani Mzimu Wodzikweza! 5/15
Rahabi—Anayesedwa Wolungama ndi Ntchito za Chikhulupiriro, 12/15
Sanaganize za Kulolera Molakwa! (Akristu Oyambirira), 11/15
Tchalitchi cha ku Latin America Chikuthedwa Nzeru, 6/15
Uchidakwa, 8/15
Utatu—Kodi Umaphunzitsidwa m’Baibulo? 10/15
Zithumwa za Mwaŵi, 9/1
Zithunzithunzi Zachipembedzo, 4/15
Zolengedwa Zatsopano Zipangidwa! 1/1
YEHOVA
Akristu Oyambirira Anagwiritsira Ntchito Dzina la Mulungu? 11/1
Dzina la Mulungu, 12/1
Kodi Yehova Ndani? 7/15
Kuthetsa Chinsinsi cha Dzina Lalikulu Koposa, 11/1
Mlengi Wathu Wamkulu ndi Ntchito Zake, 1/1
Mpatsi wa “Mphatso Iliyonse Yabwino,” 12/1
Yehova—Mulungu Wowona ndi Wamoyo, 7/15
Zochita za Yehova za Kupulumutsa Tsopano Lino, 12/1
YESU KRISTU
Kodi Anabadwa m’Nthaŵi ya Chipale? 12/15