Zisonyezero za Nkhani za mu Nsanja ya Olonda za 1996
Zosonyeza deti la kope lopezekamo nkhaniyo
BAIBULO
Nkhondo Kaamba ka Baibulo la Chispanya, 6/1
Nthano ya Chigumula Imachirikiza Mbiri ya Baibulo, 9/15
MAFUNSO OCHOKERA KWA OŴERENGA
Akristu amene ali ndi chiyembekezo cha padziko lapansi ali ndi mzimu wolingana ndi wa odzozedwa? 6/15
Atsopano akudzozedwa ndi mzimu woyera? 8/15
Chifukwa chake toʹte (pamenepo) amagwiritsiridwa ntchito kusonyeza choyambirira ndi chotsatira? 7/15
Dzina la banja lililonse (Aef 3:14, 15), 1/15
Kodi Akristu angakhululukire machimo? 4/15
Kodi munthu akhoza kuiŵala chinthu modzifunira? (Afil 3:13), 5/1
Kwanzeru kukaonana ndi sing’anga wa nthenda zamaganizo? 9/1
Ufumu wa Mulungu udze padziko lapansi? 6/1
Yesu akudziŵa deti la Armagedo? 8/1
MBONI ZA YEHOVA
Anachirikizidwa ndi Bwenzi Lawo Lalikulu Koposa (Czechoslovakia), 3/15
Chifutukuko ndi Dalitso la Yehova (kupatulira kumalikulu), 4/15
Kodi Ndinu Mpainiya Wolinganiza Zinthu? 5/15
Kufalitsa Choonadi cha Baibulo ku Portugal, 2/15
Kumaliza Maphunziro a Gileadi,6/1, 12/1
Kupuma Pantchito—Khomo Lotseguka la Ntchito Yateokrase? 7/15
Kuyenera kwa Chivomerezo Chodziŵa Kutsimikizidwanso, 11/15
Misonkhano Yachigawo ya “Atamandi Achimwemwe,” 1/15
Mkhalidwe Wochititsa Zinthu Kukula (Equatorial Guinea), 10/15
Mkupiti wa Umboni ku Greece, 4/15
Mtendere m’Dziko Lamavuto, 1/1
“Muzindikire Otere,” 6/15
“Ndiye Tchalitchi Chanu Chili Kuti?” (Mozambique), 12/15
Thangato Pakati pa Zowonongeka, 12/1
Ufulu wa Chipembedzo Uchirikizidwa ku Japan, 11/1
Umboni ku Cameroon, 8/15
Umboni ku Greenland, 6/15
Zoyenera za Wodwala Zilemekezedwa, 3/15
MOYO NDI MIKHALIDWE YACHIKRISTU
Chikristu Choyambirira ndi Boma, 5/1
Chitani Chikumbutso Moyenera, 4/1
Chitonthozo ndi Chilimbikitso—Ngale za Mbali Zambiri, 1/15
Gwiritsirani Ntchito Mwaŵi Wapadera Umenewu! 11/15
Kuchita Mogwirizana ndi Lumbiro Lanu la Ukwati! 3/1
Kukhala ndi Lingaliro Laumulungu pa Moŵa, 12/15
Kulunjika Nawo Bwino Mawu a Mulungu, 1/1
“Kumbukirani Masiku Apitawo”—Chifukwa Ninji? 12/1
Kupemphera Motani kwa Mulungu? 7/15
Kupeza Chimwemwe Popanga Ophunzira, 2/15
‘Kusamalira Nyumba ya Munthuwe’—m’Maiko Omatukuka, 10/1
Kutsanzira Mulungu Wathu Wopanda Tsankhu? 11/15
Kuuluka Pamwamba ndi Mapiko Monga Ziombankhanga, 6/15
Mmene Abusa Achikristu Amakutumikirirani, 3/15
Mphindi Yakutonthola ndi Mphindi Yakulankhula, 5/15
Mufunikiradi Kupepesa? 9/15
Mulungu, Boma, ndi Inuyo, 5/1
Yang’anani Kupyola pa Zinthu Zimene Mukuona! 2/15
Sungani Chidaliro Chili Cholimba Kufikira Mapeto, 5/1
NKHANI ZA MOYO WA ANTHU
Anatumikira Yehova Modzichepetsa (J. Booth), 6/15
Chiyembekezo cha Moyo Wanga Wonse—Kusafa Konse(H. Priest), 2/1
“Gwirirani Ntchito, Osati Chakudya Chimene Chimawonongeka” (D. Lunstrum), 4/1
Kutumikira Mulungu Wodalirika (K. Progakis), 9/1
Kutumikira Pansi pa Dzanja la Yehova Lachikondi (L. Zoumbos), 5/1
Kutumikira Yehova Monga Banja Logwirizana (A. Santoleri), 10/1
Kusumika Maso ndi Mtima pa Mphoto (E. Michael), 8/1
Mawu a Mulungu Amachita “Zozizwitsa” (T. Héon), 7/1
Ogwirizana mu Utumiki mu Nthaŵi Zabwino ndi Zoipa (M. and B. Muller), 3/1
Yehova Anakhala Nane (M. Henning), 6/1
Yehova Sanatisiye (N. Dori), 1/1
Yehova Wakhala Pobisalira Panga (P. Makris), 12/1
Zaka Zoposa 50 za ‘Kuwolokerako’’ (E. Paterakis), 11/1
NKHANI ZAZIKULU ZOPHUNZIRA
Achichepere Amene Amakumbukira Mlengi Wawo, 12/1
Achimwemwe Tsopano ndi Kosatha, 2/15
Anthu Afunikira Chidziŵitso Chonena za Mulungu, 1/15
Banja la Yehova Lili ndi Umodzi Wamtengo Wapatali, 7/15
‘Cherezani Alendo,’ 10/1
Chifukwa Chake Chipembedzo cha Dziko Chidzatha, 4/15
Chifukwa Chake Kulambira Koona Kumakhala ndi Dalitso la Mulungu, 4/15
Chilakiko cha Kulambira Koona Chayandikira, 7/1
Chilamulo cha Kristu, 9/1
Chilamulo Kristu Asanadze, 9/1
Dziperekeni pa Kuŵerenga, 5/15
Kachisi Wauzimu Wamkulu wa Yehova, 7/1
“Khalani Inunso Oyera Mtima m’Makhalidwe Anu Onse,” 8/1
Kodi Chachikulu Kopambana m’Moyo Wanu Nchiyani? 12/15
Kodi Mudzapulumuka Pamene Mulungu Achitapo Kanthu? 8/15
“Kondani Choonadi ndi Mtendere”! 1/1
Kuchereza Alendo Kwachikristu m’Dziko Logaŵanikana 10/1
Kudza kwa Yesu Kapena Kukhalapo kwa Yesu—Nchiti? 8/15
Kugaŵana Chitonthozo Chimene Yehova Amapereka, 11/1
Kukhala Mwamuna ndi Mkulu—Kulinganiza Mathayowo, 10/15
Kukhala Tate ndi Mkulu—Kukwaniritsa Mathayowo, 10/15
Khulupirirani Yehova ndi Mawu Ake, 2/1
Kupambana Chiyeso cha Kukhulupirika, 3/15
Kupereka Zake za Kaisara kwa Kaisara, 5/1
Kuphunzitsidwa Kuchita Chifuniro cha Yehova, 12/15
Kuthaŵira Kopulumukira “Chisautso Chachikulu” Chisanadze, 6/1
Kutsatira Chilamulo cha Kristu, 9/1
Madalitso Kapena Matemberero—Pali Chosankha! 6/15
Madalitso Kapena Matemberero—Zitsanzo kwa Ife Lerolino, 6/15
Makolo, Kondwerani mwa Ana Anu, 12/1
“Manja Anu Asakhale Olefuka” 3/1
Maphunziro—Agwiritsireni Ntchito Kutamanda Yehova, 2/1
Mbewu ya Njoka—Yavumbulidwa Motani? 6/1
Mmene Oyang’anira Oyendayenda Amatumikirira Monga Adindo Okhulupirika, 11/15
Mulungu ndi Kaisara, 5/1
“Mundilindire,” 3/1
‘Muyenera Kukhala Oyera Pakuti Ine Ndine Woyera,’ 8/1
Nkhosa za Yehova Zimafuna Kuzisamalira Mokoma Mtima, 1/15
‘Nyumba Yakupemphereramo Anthu a Mitundu Yonse,’ 7/1
Onse Ayenera Kudziŵerengera Mlandu kwa Mulungu, 9/15
Oyang’anira Oyendayenda—Mphatso mwa Amuna, 11/15
Pezani Chitonthozo kwa Yehova, 11/1
Sungani Umodzi m’Masiku Ano Otsiriza, 7/15
Tamandani Mfumu Yamuyaya! 4/1
“Tamandani Ya, Anthu Inu!” 4/1
Taonani Okhulupirika! 3/15
Tili ndi Chifukwa Chofuulira ndi Chimwemwe, 2/15
Ufumu wa Mulungu—Kodi Mukumvetsa Lingaliro Lake? 2/1
Umbeta—Khomo la Ntchito Yopanda Chocheukitsa, 10/15
Ŵerengani Mawu a Mulungu ndi Kumtumikira m’Choonadi, 5/15
Yehova Amapereka Mtendere ndi Choonadi Zochuluka, 1/1
Yehova Aŵerengeretu Bwino Mlandu Wanu, 9/15
NKHANI ZOSIYANASIYANA
Achimwemwe m’Dziko Lopanda Chimwemwe 1/15
Akula ndi Priskila—Banja Lopereka Chitsanzo Chabwino, 12/15
Apolo—Mlaliki wa Choonadi Chachikristu Wolankhula Mwanzeru, 10/1
Buthu Linalankhula Molimba Mtima, 5/15
Chisungiko Chenicheni—Chonulirapo Chovuta Kuchifikira, 5/15
Chisungiko Chenicheni—Tsopano ndi Kosatha, 5/15
Chitonthozo kwa Otsenderezedwa, 11/1
Chitonthozo Mkati mwa Zaka Zinayi za Nkhondo (Bosnia, Croatia), 11/1
Chiyembekezo Chabwino cha Sou, 8/1
Chiwawa Chili Ponseponse, 2/15
Chuma cha Solomo Nchokukumazidzwa? 10/15
Danieli Anatumikira Mulungu Mosalekeza, 11/15
Epafrodito—Nthumwi ya Afilipi, 8/15
Faraday—Wasayansi Ndiponso Mwamuna Wachikhulupiriro, 8/1
Filipo Abatiza Mdindo wa ku Aitiopiya, 7/15
Gamaliyeli—Anaphunzitsa Saulo wa ku Tariso, 7/15
Isitala Kapena Chikumbutso—Nchiti? 4/1
Kodi Baibulo Limaphunzitsa za Kukhulupirira Choikidwiratu? 9/1
Kodi Kuli Moyo Pambuyo pa Imfa? 10/15
Kodi Kusala Kudya Nkwachikhale? 11/15
Kodi Maloto Angalosere Mtsogolo? 10/1
Kodi Mtendere Ngwotheka? 1/1
Kodi Mulungu Amafuna Kusala Kudya? 11/15
Kodi Munapulumutsidwa? 2/1
Kodi Ndani Ayenera Kutchedwa Kuti Rabi? 7/1
‘Kodi Ndili Wofunika Pamaso pa Mulungu?’ 3/1
Kodi Sou Siimafa? 8/1
Kodi Tiyenera Kuchitanji Kuti Tipulumutsidwe? 2/1
Kubwerera Kufumbi—Motani? 9/15
Kukhala ndi Maubwenzi Okhalitsa, 3/15
Kutheratu kwa Chiwawa—Motani? 2/15
Kuunika Kuthetsa Nyengo ya Mdima, 1/15
Kuwonjezereka kwa Zochitika za Mbiri Yoipa, 4/15
Kuyendera Dziko Lolonjezedwa, 8/15
Lidiya—Wopembedza Mulungu Ndiponso Wochereza Alendo 9/15
Maphunziro Otengedwa ku Dziko Lolonjezedwa, 8/15
Mbiri Yabwino Mtsogolo! 4/15
Mmene Mulungu Amaonera Kulambira kwa Dziko Lachikristu, 7/1
Mose ndi Aroni—Alengezi Olimba Mtima, 1/15
Moyo Pambuyo pa Imfa—Motani, Kuti, Liti? 10/15
Moyo Wanu Umalamuliridwa ndi Choikidwiratu? 9/1
Ndi Wochitiridwa Tsankhu? 6/1
Nkumpatsiranji Yehova? 11/1
“Nyumba ya Davide”—Yeniyeni Kapena Yopeka? 10/15
Pamene Kugwa Masoka Achilengedwe, 12/1
Petro Alalikira pa Pentekoste, 9/15
Sikudzakhalanso Tsankhu! 6/1
Theophilus wa ku Antiokeya, 3/15
Tifunikira Mabwenzi Enieni, 3/15
“Tiphunzitseni Ife Kupemphera,” 7/15
Tiyenera Kulota, 10/1
Yona Aphunzira za Chifundo cha Yehova, 5/15
Zimene Zolengedwa “Zanzeru Mwachibadwa” Zimatiphunzitsa, 7/15
Zipembedzo Zonse Zimakondweretsa Mulungu? 9/15
OLENGEZA UFUMU AKUSIMBA
1/1, 2/1, 3/1, 4/1, 5/1, 6/1, 8/1, 9/1, 10/1, 12/1
YEHOVA
Chifukwa Chake Iye Anagwiritsira Ntchito Dzina Lalikulululo, 4/15
Kodi Kukonda Mulungu Kumatanthauzanji? 6/15
Kodi Mungathe Kumkondadi Mulungu? 6/15
Mulungu Amasamala za Inu, 3/1
Mulungu Amavomereza Kulambira Kwamtundu Uliwonse? 7/1
Senzani Yehova Nkhaŵa Yanu Nthaŵi Zonse, 4/1
Yehova—Wokonda Chilungamo ndi Chiweruzo, 3/15
YESU KRISTU
Choonadi Ponena za Yesu, 12/15
Kodi Mukanamzindikira Mesiya? 11/15
Kulabadira Mawu a Yesu Otsazikira, 3/15
Uthenga Wabwino Malinga ndi Akatswiri, 12/15