Tsamba 32
◼ Kodi n’chiyani chingakuthandizeni kukhala ndi mtendere wa mumtima ngakhale muli pa umphawi, mukudwala kapena mukuona kuti mukhoza kumwalira?
◼ Kodi kupemphera m’dzina la Yesu n’kofunika pa zifukwa zitatu ziti?
◼ N’chifukwa chiyani lilime tingaliyerekezere ndi moto?
◼ N’chifukwa chiyani Mulungu amalola kuti tizivutika?
◼ Kodi ndi mavuto ena ati amene azimayi omwe ali pantchito amakumana nawo kawirikawiri?