Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • w08 2/15 tsamba 1-2
  • Zamkatimu

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Zamkatimu
  • Nsanja ya Olonda—2008
  • Timitu
  • NKHANI ZOPHUNZIRA MLUNGU WA:
  • Cholinga cha Nkhani Zophunzira
  • M’MAGAZINI INO MULINSO:
Nsanja ya Olonda—2008
w08 2/15 tsamba 1-2

Zamkatimu

February 15, 2008

Magazini Yophunzira

NKHANI ZOPHUNZIRA MLUNGU WA:

March 17-23, 2008

Ikani Yehova Patsogolo Panu Nthawi Zonse

TSAMBA 3

NYIMBO ZOIMBA: 37, 26

March 24-30, 2008

Yendani M’njira za Yehova

TSAMBA 7

NYIMBO ZOIMBA: 138, 57

March 31, 2008–April 6, 2008

Yesu Khristu—Mmishonale Woposa Amishonale Onse

TSAMBA 12

NYIMBO ZOIMBA: 172, 72

April 7-13, 2008

Tsanzirani Mmishonale Woposa Amishonale Onse

TSAMBA 16

NYIMBO ZOIMBA: 211, 209

April 14-20, 2008

Kodi Kukhalapo kwa Khristu Kumatanthauza Chiyani kwa Inu?

TSAMBA 21

NYIMBO ZOIMBA: 168, 21

Cholinga cha Nkhani Zophunzira

Nkhani Zophunzira 1, 2 MASAMBA 3-11

Tikamasinkhasinkha nkhani za m’Baibulo, chikhulupiriro chathu chimalimba. Tikamaika Yehova patsogolo pathu, iye amayankha mapemphero athu. Kuti zimenezi zitheke, tiyenera kumvera Mulungu ndi kumukhulupirira nthawi zonse. Tikamayenda m’njira zake, tidzakhala anthu odalirika, odzichepetsa, olimba mtima ndi osamala zofuna za ena.

Nkhani Zophunzira 3, 4 MASAMBA 12-20

Yesu Khristu anali Mmishonale woposa amishonale onse. Dziwani mmene iye anaphunzitsidwira, mmene anali kuphunzitsira ndi chifukwa chimene anthu anali kumukondera. Werengani zimene tiyenera kuchita kuti titsanzire Yesu ndi kuphunzitsa mogwira mtima anthu amene timawalalikira uthenga wabwino.

Nkhani Zophunzira 5 MASAMBA 21-25

Dziwani chifukwa chimene tinganenere kuti nthawi ya kukhalapo kwa Khristu ndi yaitali. Fufuzani umboni wa m’Malemba wotithandiza kudziwa anthu a “m’badwo uwu,” umene Yesu anatchula. (Mat. 24:34) Ndipo onani chifukwa chake zilili zosatheka kuwerengetsa zaka za “m’badwo uwu.”

M’MAGAZINI INO MULINSO:

Titengerepo Phunziro Pazolakwa za Aisiraeli

TSAMBA 26

Mawu a Yehova Ndi Amoyo​—Mfundo Zazikulu za M’buku la Maliko

TSAMBA 28

Omaliza Maphunziro a Gileadi Akulimbikitsidwa Kuti “Ayambe Kukumba”

TSAMBA 31

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena