Zamkatimu
October 1, 2008
Kodi Baibulo Limalosera Zam’tsogolo?
ZIMENE ZILI M’MAGAZINI INO
3 Kodi Ndani Angadziwe Zam’tsogolo?
4 Baibulo Linaneneratu za Mesiya
6 Ulosi Wokhudza Zimene Zikuchitika Masiku Ano
8 Linaneneratu Zimene Zichitike Posachedwapa
15 Yandikirani Mulungu—“Khalani Otsanzira Mulungu”
16 Phunzitsani Ana Anu—Abale Ake a Yosefe Anachita Nsanje—Kodi Iwenso Umachita Nsanje?
22 Tsanzirani Chikhulupiriro Chawo—‘Analingalira Mawuwo Mumtima Mwake’
28 Chikhulupiriro Chinandithandiza Kupirira Mavuto
Kodi Nkhani za M’mabuku a Uthenga Wabwino N’zenizeni?
TSAMBA 12
Kodi Mungatani Kuti Mukhale Bambo Wabwino?
TSAMBA 18