Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • w08 12/15 tsamba 1-2
  • Zamkatimu

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Zamkatimu
  • Nsanja ya Olonda—2008
  • Timitu
  • NKHANI ZOPHUNZIRA MILUNGU YA:
  • Cholinga cha Nkhani Zophunzira
  • M’MAGAZINI INO MULINSO:
Nsanja ya Olonda—2008
w08 12/15 tsamba 1-2

Zamkatimu

December 15, 2008

Magazini Yophunzira

NKHANI ZOPHUNZIRA MILUNGU YA:

February 2-8, 2009

N’chifukwa Chiyani Muyenera Kusunga Umphumphu?

TSAMBA 3

NYIMBO ZOIMBA: 10, 160

February 9-15, 2009

Kodi Mudzasungabe Umphumphu?

TSAMBA 7

NYIMBO ZOIMBA: 26, 29

February 16-22, 2009

Udindo Wapadera wa Yesu Pokwaniritsa Cholinga cha Mulungu

TSAMBA 12

NYIMBO ZOIMBA: 205, 105

February 23, 2009–March 1, 2009

Chitirani Umboni Bwino Lomwe

TSAMBA 16

NYIMBO ZOIMBA: 6, 193

Cholinga cha Nkhani Zophunzira

Nkhani Zophunzira 1, 2 MASAMBA 3-11

Kodi umphumphu ndi chiyani? N’chifukwa chiyani kusunga umphumphu kuli kofunika? Kodi tingatani kuti tiyambe komanso tipitirizebe kusunga umphumphu? Kodi n’zotheka kuti munthu amene waswa umphumphu ayambirenso kuusunga? Nkhani ziwirizi zitithandiza kupeza mayankho a mafunso amenewa.

Nkhani Yophunzira 3 MASAMBA 12-16

Yesu ali ndi udindo wapadera pokwaniritsa cholinga cha Mulungu. Nkhaniyi ikufotokoza bwino mayina audindo 6 amene Yesu ali nawo. Mayina amenewa akusonyeza kuti Yesu ndi wapadera. Tionanso mmene Yesu wakwaniritsira udindo wake wapadera, ndiponso mmene tingamutsanzirire.

Nkhani Yophunzira 4 MASAMBA 16-20

Kukambirana zimene mtumwi Paulo anauza akulu a ku Efeso, zomwe zalembedwa m’chaputala 20 cha buku la Machitidwe, kutithandiza kudziwa zimene zinamuthandiza kuchitira umboni bwino lomwe. Tiphunziranso mmene tingachitire umboni bwino lomwe za uthenga wabwino komanso chifukwa chake tiyenera kuchita zimenezo.

M’MAGAZINI INO MULINSO:

Zolemba Zakale Zimatsimikizira Kuti Baibulo N’lolondola

TSAMBA 21

Ndaona Mboni za Yehova Zikuwonjezereka ku Korea

TSAMBA 23

Mawu a Yehova Ndi Amoyo​—Mfundo Zazikulu za M’makalata a Yohane ndi Yuda

TSAMBA 27

Kodi Mukukumbukira?

TSAMBA 30

Mlozera Nkhani wa Magazini a Nsanja ya Olonda a 2008

TSAMBA 31

Mafunso Ochokera kwa Owerenga

TSAMBA 32

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena