Zamkatimu
January 15, 2009
Magazini Yophunzira
NKHANI ZOPHUNZIRA MILUNGU YA:
March 2-8, 2009
‘Bwera Ukhale Wotsatira Wanga’
TSAMBA 3
NYIMBO ZOIMBA: 200, 172
March 9-15, 2009
Sangalalani Ndi Ntchito Yopanga Ophunzira
TSAMBA 7
NYIMBO ZOIMBA: 130, 211
March 16-22, 2009
Kodi Ndinu ‘Mdindo wa Kukoma Mtima kwa m’Chisomo cha Mulungu’?
TSAMBA 12
NYIMBO ZOIMBA: 50, 58
March 23-29, 2009
Taonani Mtumiki Amene Yehova Amakondwera Naye
TSAMBA 21
NYIMBO ZOIMBA: 168, 4
March 30, 2009–April 5, 2009
Mtumiki wa Yehova “Analasidwa Chifukwa cha Zolakwa Zathu”
TSAMBA 25
NYIMBO ZOIMBA: 224, 214
Cholinga cha Nkhani Zophunzira
Nkhani Zophunzira 1-3 MASAMBA 3-16
Kodi kutsatira Khristu kumatanthauza chiyani? Kumatanthauza kutsanzira makhalidwe ake apadera monga nzeru ndi kudzichepetsa. Kumatanthauzanso kukhala achangu pantchito yopanga ophunzira. Ndiponso kumatanthauza kuwakonda zenizeni okhulupirira anzathu. Nkhani zimenezi zikufotokoza zimene tingachite potsanzira Khristu m’njira zitatu zimenezi.
Nkhani Zophunzira 4, 5 MASAMBA 21-29
Nkhani ziwiri zimenezi zikufotokoza maulosi angapo a m’buku la Yesaya amene anakwaniritsidwa pa Yesu Khristu. Kuphunzira maulosi amenewa kutithandiza kuyamikira kwambiri zimene Yehova ndi Yesu anatichitira mwa imfa ndi kuukitsidwa kwa Yesu. Choncho, nkhani zimenezi zitithandiza kuti tikonzekere m’maganizo ndi m’mitima yathu kuti tidzapezeke pamwambo wokumbukira imfa ya Yesu, umene udzachitike madzulo a pa April 9, 2009.
M’MAGAZINI INO MULINSO:
“Njira Ndi Iyi, Yendani Inu Mmenemo”
TSAMBA 17
Mawu a Yehova Ndi Amoyo—Mfundo Zazikulu za M’buku la Chivumbulutso—Gawo 1
TSAMBA 30