Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • w09 2/1 tsamba 32
  • Kodi Mungafune Kukuchezerani?

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Kodi Mungafune Kukuchezerani?
  • Nsanja ya Olonda—2009
Nsanja ya Olonda—2009
w09 2/1 tsamba 32

Kodi Mungafune Kukuchezerani?

Ngakhale m’dziko lamavutoli, mungakhalebe osangalala podziwa zenizeni zimene Baibulo limaphunzitsa pa nkhani ya Mulungu, Ufumu wake, ndi cholinga chimene iye ali nacho chakuti anthu adzakhale ndi moyo wabwino kwambiri. Ngati mukufuna kudziwa zambiri kapena kuti wina aziphunzira nanu Baibulo panyumba panu kwaulere, lembani kalata n’kuitumiza kwa Mboni za Yehova, P.O. Box 30749, Lilongwe 3, kapena gwiritsani ntchito adiresi yoyenerera pa maadiresi amene ali patsamba 4.

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena