Tsamba 32
◼ Kodi dzina la Mulungu ndi ndani? Onani tsamba 6.
◼ Kodi ndani kwenikweni akulamulira dzikoli? Onani tsamba 8.
◼ Ngati muli ndi ana, kodi n’chifukwa chiyani ndi bwino kukhala ndi nthawi yocheza ndi mwamuna kapena mkazi wanu? Onani tsamba 11.
◼ Kodi mayi amene ankazembetsa miyala ya diamondi komanso kuwabera abwana ake anasintha bwanji kukhala woona mtima? Onani masamba 26 ndi 27.
◼ Kodi n’chifukwa chiyani Mboni za Yehova sizigwiritsa ntchito mafano polambira? Onani masamba 30 ndi 31.