Zamkatimu
March 1, 2009
Kodi Mulungu Analemberatu Zochitika Zonse za pa Moyo Wanu?
ZIMENE ZILI M’MAGAZINI INO
4 Chilichonse Chili ndi Nthawi
10 Anthu Amene Anavutika ndi Chimphepo ku Myanmar Anathandizidwa
15 Yandikirani Mulungu—“Ndidziwa Zowawitsa Zawo”
16 Mtengo ‘Umene Tsamba Lake Silifota’
18 Kalata Yochokera ku Ireland
20 Munthu Sakhala ndi Moyo ndi Chakudya Chokha—Mmene Ndinapulumukira M’ndende za Chipani cha Nazi
25 Mzinda wa Korinto “Unali ndi Magombe Awiri Akeake”
30 Malo a Msonkhano Wachigawo wa 2009 Wakuti “Khalani Maso”
32 Tsiku Lofunika Kwambiri M’mbiri Yonse ya Anthu
Mfundo Zisanu Zotilimbikitsa Kuopa Mulungu Osati Anthu
TSAMBA 12
Zoti Achinyamata Achite—Kuukitsidwa kwa Lazaro
TSAMBA 24