Zamkatimu
APRIL 1, 2009
Kodi Kubadwa Mwatsopano Kumatanthauza Chiyani?
ZIMENE ZILI M’MAGAZINI INO
3 Kodi Kubadwanso Ndiyo Njira Yopezera Chipulumutso?
5 Kodi Kubadwa Mwatsopano N’kofunika Motani?
5 Kodi Kubadwa Mwatsopano Ndi Nkhani Yoti Munthu Amachita Kusankha Yekha?
7 Kodi Kubadwa Mwatsopano Kuli N’cholinga Chotani?
8 Kodi Kubadwa Mwatsopano Kumachitika Motani?
10 Kodi Kubadwa Mwatsopano Kumakwaniritsa Zinthu Zotani?
11 Ulamuliro wa Anthu Ochepa Udzabweretsa Madalitso kwa Anthu Ambiri
20 Mawu a Mulungu Ndi Amoyo Ngakhale M’chinenero Chakufa
24 Phunzitsani Ana Anu—Yoasi Anasiya Kutumikira Yehova Chifukwa Chocheza ndi Anthu Ochita Zoipa
27 Kodi Kusala Kudya Kumathandiza Munthu Kuyandikira kwa Mulungu?
30 Akuluakulu a Katolika Akufuna Kusiyiratu Kugwiritsa Ntchito Dzina la Mulungu
Tsanzirani Chikhulupiriro Chawo—Anaphunzira Kufunika Kochitira Ena Chifundo
TSAMBA 14
Yandikirani Mulungu—Atate wa Ana Amasiye
TSAMBA 31