Zamkatimu
April 15, 2009
Magazini Yophunzira
NKHANI ZOPHUNZIRA MILUNGU YA:
June 1-7, 2009
Yobu Analemekeza Dzina la Yehova
TSAMBA 3
NYIMBO ZOIMBA: 197, 41
June 8-14, 2009
Umphumphu Wanu Umakondweretsa Mtima wa Yehova
TSAMBA 7
NYIMBO ZOIMBA: 160, 138
June 15-21, 2009
Chilengedwe Chimasonyeza Nzeru za Yehova
TSAMBA 15
NYIMBO ZOIMBA: 79, 84
June 22-28, 2009
TSAMBA 24
NYIMBO ZOIMBA: 205, 150
June 29, 2009–July 5, 2009
Kuzindikira Yesu Monga Davide Wamkulu Ndiponso Solomo Wamkulu
TSAMBA 28
NYIMBO ZOIMBA: 168, 209
Cholinga cha Nkhani Zophunzira
Nkhani Zophunzira 1, 2 MASAMBA 3-11
Nkhani zimenezi zikufotokoza chifukwa chake Yehova analola Satana kuti abweretsere Yobu mayesero osiyanasiyana. Zikufotokozanso chimene chinathandiza Yobu kusunga umphumphu wake. Komanso zikufotokoza zimene ifeyo tingachite kuti tikhalebe okhulupirika monga Yobu ndi kukondweretsa mtima wa Yehova.
Nkhani Yophunzira 3 MASAMBA 15-19
Zinthu zimene Yehova analenga zimasonyeza makhalidwe ake osiyanasiyana. Tingaphunzire zinthu zambiri ngati titamaganizira zimene iye analenga. M’nkhaniyi, tikambirana zinthu zinayi zimene Yehova analenga ndiponso zimene tingaphunzirepo.
Nkhani Zophunzira 4, 5 MASAMBA 24-32
Nkhani za m’Baibulo za anthu ena okhulupirika amene anakhalapo Yesu asanabadwe zimasonyeza kuti pali zinthu zina zofanana kwambiri pakati pa anthuwo ndi Yesu. M’nkhani ziwirizi, tikambirana za Mose, Davide ndi Solomo ndipo tiona mmene nkhani za moyo wawo zingatithandizire kuzindikira udindo wa Yesu pokwaniritsa cholinga cha Mulungu.
M’MAGAZINI INO MULINSO:
Mafunso Ochokera kwa Owerenga—Ngati mwana wabadwa wakufa, kodi pali chiyembekezo chakuti adzauka?
TSAMBA 12
TSAMBA 14
Kodi Mungakatumikire Kumene Kukufunika Ofalitsa Ufumu Ambiri?
TSAMBA 20