Zamkatimu
May 15, 2009
Magazini Yophunzira
NKHANI ZOPHUNZIRA MILUNGU YA:
July 6-12, 2009
Yesetsani Kukula Mwauzimu Chifukwa “Tsiku Lalikulu la Yehova Lili Pafupi”
TSAMBA 9
NYIMBO ZOIMBA: 123, 174
July 13-19, 2009
Achinyamata, Yesetsani Kuti Kupita Kwanu Patsogolo Kuonekere
TSAMBA 13
NYIMBO ZOIMBA: 42, 56
July 20-26, 2009
Angelo Ndiwo “Mizimu Yotumikira Anthu”
TSAMBA 21
NYIMBO ZOIMBA: 6, 5
July 27, 2009–August 2, 2009
N’chifukwa Chiyani Tiyenera Kutsatira “Khristu”?
TSAMBA 28
NYIMBO ZOIMBA: 121, 134
Cholinga cha Nkhani Zophunzira
Nkhani Zophunzira 1 ndi 2 MASAMBA 9-17
Nkhani yophunzira yoyamba ikunena za kufunika kokula mwauzimu ndiponso zimene munthu angachite kuti akule mwauzimu. Nkhani yachiwiri ikufotokoza zimene achinyamata achikhristu angachite kuti athane ndi zinthu zimene zingawalepheretse kukula mwauzimu.
Nkhani Yophunzira 3 MASAMBA 21-25
Kuphunzira Malemba kungatithandize kudziwa mmene angelo amagwirira ntchito yawo monga “mizimu yotumikira anthu.” Nkhaniyi ikusonyeza zimene angelo akuchita pothandiza Akhristu masiku ano. Itithandizanso kuona zimene tingaphunzire kwa angelo okhulupirika.
Nkhani Yophunzira 4 MASAMBA 28-32
Yesu Khristu anauza anthu amene ankamumvetsera kuti amutsatire mosalekeza. Nkhani ino ikufotokoza zifukwa zisanu zimene zingatithandize kukhala ndi mtima wofunitsitsa kutsatira “Khristu” nthawi zonse.
M’MAGAZINI INO MULINSO:
TSAMBA 3
Kodi Mapeto Ayenera Kudzakupezani Muli Kuti?
TSAMBA 6
TSAMBA 18
Amuna, Tsanzirani Chikondi cha Khristu
TSAMBA 19
Tsanzirani Kukhulupirika kwa Itai
TSAMBA 26