Zamkatimu
August 1, 2009
Kodi Mungatani Kuti Musankhe Chipembedzo Chabwino?
ZIMENE ZILI M’MAGAZINI INO
3 Kodi Zipembedzo Zonse N’zabwino?
5 Chipembedzo Chabwino Chimalimbikitsa Anthu Kukhala ndi Makhalidwe Abwino
6 Chipembedzo Chabwino Chimalimbikitsa Anthu Kukondana
8 Chipembedzo Chabwino Chimalimbikitsa Anthu Kulemekeza Mawu a Mulungu
13 Kodi Mumalola Kuti Mulungu Azikulankhulani Tsiku Lililonse?
24 Phunzitsani Ana Anu—Rahabi Anamvetsera Uthenga
26 Yandikirani Mulungu—Yehova Amakonda Anthu Ofatsa
30 Zimene Owerenga Amafunsa—Kodi Mulungu Amafuna Kuti Ndizipereka Ndalama Zingati?
Chinsinsi cha Banja Losangalala—Muzigwiritsa Ntchito Ndalama Mwanzeru
TSAMBA 10
Zimene Tikuphunzira kwa Yesu—Ponena za Tsogolo la Anthu
TSAMBA 22