Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • w09 8/15 tsamba 1-2
  • Zamkatimu

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Zamkatimu
  • Nsanja ya Olonda—2009
  • Timitu
  • NKHANI ZOPHUNZIRA MILUNGU YA:
  • Cholinga cha Nkhani Zophunzira
  • M’MAGAZINI INO MULINSO:
Nsanja ya Olonda—2009
w09 8/15 tsamba 1-2

Zamkatimu

August 15, 2009

Magazini Yophunzira

NKHANI ZOPHUNZIRA MILUNGU YA:

September 28, 2009–October 4, 2009

Mulungu Anapereka Chiyembekezo cha Moyo Wosatha Padziko Lapansi

TSAMBA 3

NYIMBO ZOIMBA: 76, 222

October 5-11, 2009

Kodi Khristu Anaphunzitsa za Chiyembekezo cha Moyo Wosatha Padziko Lapansi?

TSAMBA 7

NYIMBO ZOIMBA: 187, 15

October 12-18, 2009

Anthu Anayambiranso Kukhala ndi Chiyembekezo cha Moyo Wosatha Padziko Lapansi

TSAMBA 12

NYIMBO ZOIMBA: 4, 220

October 19-25, 2009

“Khalanibe M’chikondi cha Mulungu”

TSAMBA 18

NYIMBO ZOIMBA: 114, 85

Cholinga cha Nkhani Zophunzira

Nkhani Zophunzira 1-3 MASAMBA 3-16

Nkhani zimenezi zikufotokoza zifukwa za m’Malemba zokhalira ndi chiyembekezo cha moyo wosatha padziko lapansi. Zidzalimbitsa chikhulupiriro chanu pa chiyembekezo chimenechi, chomwe chimasiyanitsa Akhristu oona ndi Matchalitchi Achikhristu. Kenako, chikhulupiriro chanu cholimbacho chidzakuthandizani kukhala wosangalala ndiponso wolimba mtima polankhula za chiyembekezo chanu.

Nkhani Yophunzira 4 MASAMBA 18-22

Nkhani imeneyi ikufotokoza njira zitatu zimene zingatithandize kukhalabe m’chikondi cha Mulungu. (Yuda 21) Njira zake ndi izi: (1) Kukonda anthu amene Yehova amawakonda, (2) kulemekeza ulamuliro ndiponso (3) kuyesetsa kukhalabe oyera pamaso pa Yehova.

M’MAGAZINI INO MULINSO:

Anapeza Chuma Chobisika

TSAMBA 16

Kodi Mukukumbukira?

TSAMBA 23

‘Yehova Wawalitsa Nkhope Yake pa Iwo’

TSAMBA 24

Pewani Zosokoneza ‘M’tsiku la Uthenga Wabwino’

TSAMBA 28

Ngati Munatumikirapo pa Udindo Wina Mumpingo, Kodi Mungatumikirenso?

TSAMBA 30

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena