Zamkatimu
December 15, 2009
Magazini Yophunzira
NKHANI ZOPHUNZIRA MILUNGU YA:
February 1-7, 2010
Kupita Kwanu Patsogolo Kuzionekera
TSAMBA 11
NYIMBO ZOIMBA: 45, 17
February 8-14, 2010
Khalanibe ndi Chimwemwe Mukamakumana ndi Mavuto
TSAMBA 15
NYIMBO ZOIMBA: 28, 14
February 15-21, 2010
Mesiya Ndiye Njira Yopulumutsira Anthu
TSAMBA 20
NYIMBO ZOIMBA: 12, 5
February 22-28, 2010
Khalani ndi Chikondi Chimene Sichitha Konse
TSAMBA 24
NYIMBO ZOIMBA: 3, 50
Cholinga cha Nkhani Zophunzira
Nkhani Zophunzira 1, 2 MASAMBA 11-19
Akhristu onse, amuna, akazi ndiponso ana, akhoza kusonyeza kuti akupita patsogolo mwauzimu. Nkhanizi zifotokoza mmene tingachitire zimenezi. Zifotokozanso kuti tingathe kukhala achimwemwe ngakhale pamene tikukumana ndi mavuto.
Nkhani Yophunzira 3 MASAMBA 20-24
Baibulo lili ndi umboni wosonyeza kuti Yesu ndiye Mesiya wolonjezedwa. Yehova anatuma Mwana wake kuti abwere padziko lapansi kudzayeretsa dzina Lake ndi kusonyeza kuti Iye ndiye woyenera kulamulira ndiponso kuti adzawombola anthu omvera ku uchimo ndi imfa. Zimenezi ziyenera kukhudza utumiki wathu.
Nkhani Yophunzira 4 MASAMBA 24-28
Kodi tingakulitse bwanji chikondi chathu pa Yehova ndi Yesu. Kodi chikondi chingapirire bwanji zinthu zonse? Kodi mawu akuti chikondi sichitha nthawi zonse amatanthauza chiyani? Nkhani yofotokoza lemba la chaka cha 2010 imeneyi idzayankha mafunso amenewa.
M’MAGAZINI INO MULINSO:
TSAMBA 3
Kodi Mungawolokere ku Makedoniya?
TSAMBA 4
Otanganidwa Koma Osangalala Potumikira Mulungu
TSAMBA 8
Baibulo Lifika ku Chilumba cha Madagascar
TSAMBA 29
Mlozera Nkhani wa Magazini a Nsanja ya Olonda a 2009
TSAMBA 32