Zamkatimu
January 15, 2010
Magazini Yophunzira
NKHANI ZOPHUNZIRA MILUNGU YA:
March 1-7, 2010
N’chifukwa Chiyani Muyenera Kudzipereka kwa Yehova?
TSAMBA 3
NYIMBO ZOIMBA: 7, 27
March 8-14, 2010
Ndife Anthu a Yehova Chifukwa cha Chisomo Chake
TSAMBA 7
NYIMBO ZOIMBA: 31, 16
March 15-21, 2010
Sonyezani Kuti Ndinu Wotsatira Weniweni wa Khristu
TSAMBA 12
NYIMBO ZOIMBA: 40, 25
March 22-28, 2010
Ulamuliro wa Satana Utha Posachedwa
TSAMBA 24
NYIMBO ZOIMBA: 46, 49
March 29, 2010–April 4, 2010
Yehova Ndiye Woyeneradi Kulamulira
TSAMBA 28
NYIMBO ZOIMBA: 30, 14
Cholinga cha Nkhani Zophunzira
NKHANI ZOPHUNZIRA 1, 2 MASAMBA 3-11
Nkhani zimenezi zikufotokoza zimene kudzipereka kwa Yehova kumatanthauza ndiponso chifukwa chake tiyenera kudzipereka. Tikambirananso chifukwa chake sitiyenera kukayika kuti tingathe kuchita zimene Yehova amafuna. Komanso, tiona madalitso amene anthu onse a Yehova amapeza.
NKHANI YOPHUNZIRA 3 MASAMBA 12-16
Nkhani imeneyi ikufotokoza mfundo zisanu zofunika kwambiri zimene tiyenera kuyesetsa kutsanzira Khristu. Tikamachita zimenezi, tidzasonyeza kuti ndife otsatira Khristu enieni, ndipo tidzatha kuthandiza anthu onga nkhosa kuzindikira mpingo woona wachikhristu.
NKHANI ZOPHUNZIRA 4, 5 MASAMBA 24-32
Nkhani yachinayi ikufotokoza chifukwa chake ulamuliro wa anthu wosadalira Mulungu walephera ndiponso mmene wasonyezera kuti ulamuliro wa Yehova ndi woyenera. Nkhani yachisanu ikufotokoza mmene tingasonyezere kuti tikuvomereza ulamuliro wa Yehova.
M’MAGAZINI INO MULINSO:
Thandizani Ana Anu Kulimbana ndi Mavuto Awo 16
Muzilemekeza Mulungu Tsiku ndi Tsiku 21