Zamkatimu
February 15, 2010
Magazini Yophunzira
NKHANI ZOPHUNZIRA MILUNGU YA:
April 5-11, 2010
‘Lankhulani Mawu a Mulungu Molimba Mtima’
TSAMBA 5
NYIMBO ZOIMBA: 33, 47
April 12-18, 2010
Gwiritsani Ntchito Mwaluso “Lupanga la Mzimu”
TSAMBA 10
NYIMBO ZOIMBA: 44, 37
April 19-25, 2010
“Mzimu ndi Mkwatibwi Akunenabe Kuti: ‘Bwera!’”
TSAMBA 14
NYIMBO ZOIMBA: 47, 55
April 26, 2010–May 2, 2010
Tikukulandirani ku Moyo Wabwino Koposa!
TSAMBA 24
NYIMBO ZOIMBA: 40, 32
Cholinga cha Nkhani Zophunzira
NKHANI ZOPHUNZIRA 1-3 MASAMBA 5-18
Nkhani zophunzira zimenezi, zikufotokoza mmene mzimu woyera umatithandizira pa utumiki wathu. Zikusonyezanso mmene mzimu wa Mulungu umatithandizira kulankhula molimba mtima, kuphunzitsa mwaluso ndiponso kulalikira nthawi zonse.
NKHANI YOPHUNZIRA 4 MASAMBA 24-28
Timakhala moyo wabwino koposa tikamachita zimene Yehova amafuna ndiponso tikamamvera Yesu. Nkhaniyi ikufotokoza madalitso amene anthu omwe anadzipereka kwa Mulungu ndipo anabatizidwa, amakhala nawo. Ikufotokozanso zimene tiyenera kuchita kuti tipitirizebe kukhala m’choonadi.
M’MAGAZINI INO MULINSO:
Kodi Mumaona Kuti Yehova Ndi Atate Wanu? 3
Musalole Mabodza a Satana Kukusokonezani Maganizo 19
Mafunso Ochokera kwa Owerenga 22
“Mwana Ali ndi Ufulu Wokula Mwauzimu” 29
Buku Lothandiza Achinyamata Kukumbukira Mlengi Wawo 30