Zamkatimu
March 15, 2010
Magazini Yophunzira
NKHANI ZOPHUNZIRA MILUNGU YA:
May 3-9, 2010
Kubatizidwa M’dzina la Atate, ndi la Mwana ndi la Mzimu Woyera
TSAMBA 10
NYIMBO ZOIMBA: 48, 7
May 10-16, 2010
Muziyenda mwa Mzimu Kuti Mukwaniritse Kudzipereka Kwanu
TSAMBA 14
NYIMBO ZOIMBA: 18, 51
May 17-23, 2010
“Olungama Adzawala Ngwee Ngati Dzuwa”
TSAMBA 19
NYIMBO ZOIMBA: 14, 30
May 24-30, 2010
TSAMBA 24
NYIMBO ZOIMBA: 30, 43
Cholinga cha Nkhani Zophunzira
NKHANI ZOPHUNZIRA 1, 2 MASAMBA 10-18
Nkhani ziwirizi zitithandiza kumvetsa kufunika kwa kubatizidwa “m’dzina la Atate, ndi la Mwana ndi la mzimu woyera.” (Mat. 28:19) M’nkhanizi muli mfundo zimene zingakuthandizeni kukwaniritsa kudzipereka kwanu.
NKHANI ZOPHUNZIRA 3, 4 MASAMBA 19-28
M’fanizo lake la tirigu ndi namsongole, Yesu anafotokoza zimene zidzachitikire “ana a ufumu.” Kodi tirigu akuimira ndani, nanga namsongole akuimira ndani? Kodi fanizo limeneli likukwaniritsidwa bwanji masiku ano? Kodi limangonena za odzozedwa okha?
M’MAGAZINI INO MULINSO NKHANI IZI:
Khalanibe Paubwenzi ndi Mulungu Ngakhale Zinthu Zitasintha 3
Maliko ‘Anali Wofunika Potumikira’ 6
Mafunso Ochokera kwa Owerenga 28
Khalanibe ‘Oyera Mtima’ Masiku Ovuta Ano 30
[Mawu a Chithunzi patsamba 2]
By permission of the Israel Museum, Jerusalem