Zamkatimu
June 15, 2010
Magazini Yophunzira
NKHANI ZOPHUNZIRA MILUNGU YA:
July 26, 2010–August 1, 2010
Khalani Otetezeka M’gulu la Anthu a Mulungu
TSAMBA 6
NYIMBO ZOIMBA: 16, 31
August 2-8, 2010
TSAMBA 10
NYIMBO ZOIMBA: 50, 53
August 9-15, 2010
“Pitirizani Kugonjetsa Choipa” mwa Kupewa Kupsa Mtima
TSAMBA 15
NYIMBO ZOIMBA: 52, 39
August 16-22, 2010
Kulankhula Mwaulemu Kumathandiza Kuti Tizikhala Bwino ndi Ena
TSAMBA 20
NYIMBO ZOIMBA: 19, 35
August 23-29, 2010
Kuchita Zinthu Zauzimu Kumatsitsimula
TSAMBA 25
NYIMBO ZOIMBA: 22, 48
Cholinga cha Nkhani Zophunzira
NKHANI ZOPHUNZIRA 1, 2 MASAMBA 6-14
Nkhani zimenezi zitithandiza kuti tiziyamikira kwambiri madalitso amene timapeza chifukwa chokhala mumpingo wachikhristu. Mulinso mfundo zimene zingatithandize ifeyo patokha kuona mmene tingathandizire abale ndi alongo anthu mumpingo.
NKHANI ZOPHUNZIRA 3, 4 MASAMBA 15-24
Nkhani ziwiri zimenezi zikufotokoza mmene kutsatira mfundo za m’Baibulo kungatithandizire kukhala mwamtendere ndi anthu ena ngakhale kuti tonse ndife opanda ungwiro. Zikufotokozanso kuti kulankhulana mwaulemu kungathandize kwambiri kuti tizikhala bwino ndi anthu.
NKHANI YOPHUNZIRA 5 MASAMBA 25-29
Nkhani imeneyi itithandiza kudziwa mmene tingapezere chimwemwe chosatha ndiponso chokhalitsa. Anthu m’dzikoli ali ndi maganizo olakwika pa zinthu zimene zimatsitsimula ndipo amakonda kwambiri zofuna za mtima wawo. Koma anthu a Mulungu amatsitsimulidwa akamachita zinthu zauzimu.
M’MAGAZINI INO MULINSO NKHANI IZI:
Ogwirizana Chifukwa cha Chikondi Lipoti la Msonkhano Wapachaka 3
Zimene Mungachite Ngati Mwamuna Kapena Mkazi Wanu Ali Wosakhulupirika 29