Zamkatimu
July 15, 2010
Magazini Yophunzira
NKHANI ZOPHUNZIRA MILUNGU YA:
August 30, 2010–September 5, 2010
Kodi pa Tsiku la Yehova Padzachitika Zotani?
TSAMBA 3
NYIMBO ZOIMBA: 30, 40
September 6-12, 2010
“Lingalirani za Mtundu wa Munthu Amene Muyenera Kukhala”
TSAMBA 7
NYIMBO ZOIMBA: 48, 29
September 13-19, 2010
Muzigwira Nawo Mokwanira Ntchito Yokolola Mwauzimu
TSAMBA 16
NYIMBO ZOIMBA: 45, 28
September 20-26, 2010
“Mzimu Umafufuza . . . Zinthu Zozama za Mulungu”
TSAMBA 20
NYIMBO ZOIMBA: 38, 20
Cholinga cha Nkhani Zophunzira
NKHANI ZOPHUNZIRA 1, 2 MASAMBA 3-11
M’kalata yake yachiwiri, mtumwi Petulo anasonyeza kuti ankadera nkhawa kwambiri Akhristu a m’masiku otsiriza. Nkhani ziwiri zimenezi zitithandiza kuti tizikumbukira tsiku la Yehova nthawi zonse. Tikambirana zinthu zimene tiyenera kupewa ndiponso zimene tiyenera kuchita pokonzekera tsiku lalikulu la Yehova.
NKHANI YOPHUNZIRA 3 MASAMBA 16-20
Tikukhala m’nthawi imene ntchito yaikulu yokolola mwauzimu ikuchitika. Kodi tiyenera kukhala ndi makhalidwe ati, kuti tizigwira nawo mokwanira ntchito yokololayi? Ngakhale pamene zinthu pa moyo wathu sizili bwino, kodi tingatani kuti tizigwirabe nawo mokwanira ntchito yolalikira? Nkhaniyi ikuyankha mafunso amenewa.
NKHANI YOPHUNZIRA 4 MASAMBA 20-24
Nkhaniyi ikufotokoza zimene aliyense payekha angachite kuti apindule ndi zimene mzimu wa Mulungu ukuchita potithandiza kumvetsa Mawu ake.
M’MAGAZINI INO MULINSO NKHANI IZI:
Thandizani Ana Anu Kuti Azikonda Kuwerenga ndi Kuphunzira 25
‘Pitiriza Kudzipereka pa Kuphunzitsa’ 29
Kukhala Tcheru Kumakhala ndi Zotsatira Zabwino 32