Zamkatimu
August 15, 2010
Magazini Yophunzira
NKHANI ZOPHUNZIRA MILUNGU YA:
September 27, 2010–October 3, 2010
Kodi Yesu Amasonyeza Bwanji Chilungamo cha Mulungu?
TSAMBA 8
NYIMBO ZOIMBA: 46, 49
October 4-10, 2010
TSAMBA 12
NYIMBO ZOIMBA: 31, 30
October 11-17, 2010
Muzitsatira Lamulo la Kukoma Mtima Polankhula
TSAMBA 21
NYIMBO ZOIMBA: 35, 50
October 18-24, 2010
Kodi Ndani Angathandize Anthu Ovutika?
TSAMBA 28
NYIMBO ZOIMBA: 38, 23
Cholinga cha Nkhani Zophunzira
NKHANI ZOPHUNZIRA 1, 2 MASAMBA 8-16
M’nkhani ino tiphunzira mmene Satana anatsutsira Mulungu. Tiona mmene Yesu anasonyezera kuti Yehova ndi woyenera kulamulira. Tionanso zimene Yesu anafunika kuchita kuti apereke nsembe ya dipo komanso mmene dipolo lingakupulumutsireni.
NKHANI YOPHUNZIRA 3 MASAMBA 21-25
M’nkhaniyi tiphunzira tanthauzo la kukoma mtima ndiponso mmene kumakhudzira kalankhulidwe kathu. Tionanso zimene tingachite kuti tsiku lililonse tizilankhula mokoma mtima.
NKHANI YOPHUNZIRA 4 MASAMBA 28-32
Salmo 72 limasonyeza bwino zimene zidzachitike mu Ulamulira wa zaka 1,000 wa Mwana wa Mulungu, Yesu Khristu. Mudzalimbikitsidwa kuphunzira nkhani imeneyi ndiponso kuganizira mmene Yehova adzagwiritsire ntchito Solomo Wamkulu populumutsa anthu osowa thandizo.
M’MAGAZINI INO MULINSO NKHANI IZI:
Pewani Kuyendera Maganizo a Anthu Ena 3
Mafunso Ochokera kwa Owerenga 6
N’chifukwa Chiyani Muyenera Kusunga Nthawi? 25