Zamkatimu
October 15, 2010
Magazini Yophunzira
NKHANI ZOPHUNZIRA MILUNGU YA:
November 29, 2010–December 5, 2010
“Ndani Akudziwa Maganizo a Yehova?”
TSAMBA 3
NYIMBO ZOIMBA: 11, 51
December 6-12, 2010
Pitirizani Kufunafuna Choyamba “Chilungamo Chake”
TSAMBA 7
NYIMBO ZOIMBA: 40, 22
December 13-19, 2010
Kodi Mumakhala Patsogolo Posonyeza Ulemu kwa Akhristu Anzanu?
TSAMBA 16
NYIMBO ZOIMBA: 31, 9
December 20-26, 2010
Kodi Mumathandiza Kuti Misonkhano Yachikhristu Ikhale Yolimbikitsa?
TSAMBA 20
NYIMBO ZOIMBA: 20, 34
Cholinga cha Nkhani Zophunzira
NKHANI ZOPHUNZIRA 1, 2 MASAMBA 3-11
Nkhanizi zitithandiza kuona zimene tingachite kuti tikhale pa ubwenzi wabwino ndi Yehova mwa kuphunzira za Yesu. Zikufotokozanso tanthauzo la chilungamo cha Mulungu, chifukwa chake tiyenera kuchifunafuna choyamba, ndiponso chifukwa chake sitiyenera kuweruza Yehova pogwiritsa ntchito mfundo zathu.
NKHANI YOPHUNZIRA 3 MASAMBA 16-20
Kodi chimafunika n’chiyani kuti tizilemekeza Akhristu anzathu? N’chifukwa chiyani tiyenera kuwalemekeza? Kodi tingatani kuti tikhale patsogolo pa nkhani yosonyeza ulemu? Amenewa ndi ena mwa mafunso amene tikambirane mu nkhaniyi.
NKHANI YOPHUNZIRA 4 MASAMBA 20-25
Nkhaniyi ikufotokoza zimene otsogolera pa misonkhano yachikhristu komanso ena onse angachite kuti misonkhano yathu izikhala yolimbikitsa. Ikufotokozanso zinthu zina zimene zasintha m’magazini yophunzira.
M’MAGAZINI INO MULINSO NKHANI IZI:
Kodi Yehova Amaona Bwanji Kupereka Zifukwa Pofuna Kudzikhululukira 12
Thandizani Ana Kulidziwa Bwino Gulu la Yehova 25
Ndimayesetsa Kukhala ndi Zochita Zambiri M’gulu la Yehova 29
“Kabuku Kamene Kamandithandiza Kuwafika Anthu pa Mtima” 32