Zamkatimu
November 15, 2010
Magazini Yophunzira
NKHANI ZOPHUNZIRA MILUNGU YA:
December 27, 2010–January 2, 2011
Achinyamata, Muzitsogoleredwa ndi Mawu a Mulungu
TSAMBA 3
NYIMBO ZOIMBA: 37, 22
January 3-9, 2011
Achinyamata, Pewani Kutengera Zochita Za Anzanu
TSAMBA 7
NYIMBO ZOIMBA: 24, 52
January 10-16, 2011
Achinyamata, Kodi Moyo Wanu Mudzaugwiritsa Ntchito Bwanji?
TSAMBA 12
NYIMBO ZOIMBA: 1, 11
January 17-23, 2011
Yehova Ndiye Ambuye Wathu Wamkulu Koposa
TSAMBA 24
NYIMBO ZOIMBA: 23, 51
January 24-30, 2011
Tidzayenda Mogwirizana ndi Mtima Wathu Wosagawanika
TSAMBA 28
NYIMBO ZOIMBA: 29, 45
Cholinga cha Nkhani Zophunzira
NKHANI ZOPHUNZIRA 1-3 MASAMBA 3-16
Nkhani izi zakonzedwa kuti zithandize achinyamata. Nkhani yoyamba ikusonyeza zimene achinyamata angachite kuti azitsogoleredwa ndi malangizo opezeka m’Mawu a Mulungu, Baibulo. Nkhani yachiwiri ikusonyeza mmene angapewere kutengera zochita za anzawo. Nkhani yomaliza ikufotokoza zolinga zimene achinyamata angakhale nazo ndiponso zimene angazikwaniritsedi.
NKHANI ZOPHUNZIRA 4, 5 MASAMBA 24-32
M’nkhanizi tiphunzira zimene tingachite kuti tikhale kumbali ya ulamuliro wa Yehova Mulungu. Tiphunziranso zimene tingachite kuti tikhale ndi mtima wosagawanika. Tikambirana zinthu zimene zinachitika pa moyo wa Yobu yemwe anali wolungama. Nkhani zimenezi zitithandiza kukhala ndi mtima wosagawanika komanso kuona kuti Yehova ndi Ambuye wathu Wamkulu ngati mmene Yobu ndi atumiki ena a m’mbuyomu anachitira.
M’MAGAZINI INO MULINSO NKHANI IZI:
Yehova Amamva Kulira kwa Anthu Amtima Wachisoni 17
‘Aliyense Apereke Chopereka kwa Yehova’ 20
Mafunso Ochokera kwa Owerenga 22
Zabwino ‘Zimene Anachita Zapita Naye Limodzi’ 23