Zamkatimu
January 15, 2011
Magazini Yophunzira
NKHANI ZOPHUNZIRA MILUNGU YA:
February 28, 2011–March 6, 2011
‘Pezani Chitetezo M’dzina la Yehova’
TSAMBA 3
March 7-13, 2011
Muzilemekeza Ukwati Monga Mphatso Yochokera kwa Mulungu
TSAMBA 13
March 14-20, 2011
Muzigwiritsa Ntchito Mwanzeru Nthawi Imene Simuli pa Banja
TSAMBA 17
March 21-27, 2011
Mzimu Woyera Umatipatsa Mphamvu Yolimbana ndi Mayesero Ndiponso Zofooketsa
TSAMBA 22
March 28, 2011–April 3, 2011
Mzimu Woyera Umatipatsa Mphamvu Yolimbana ndi Vuto Lililonse
TSAMBA 26
Cholinga cha Nkhani Zophunzira
NKHANI YOPHUNZIRA 1 MASAMBA 3-7
Kodi tingapeze kuti chitetezo m’masiku ovuta ano? Mawu a Mulungu amanena kuti tikhoza kupeza chitetezo m’dzina la Yehova. M’nkhaniyi tikambirana mmene tingapezere chitetezo masiku ano komanso “tsiku lalikulu la Yehova” likadzafika. Nkhaniyi ikufotokoza bwino lemba la chaka cha 2011.
NKHANI ZOPHUNZIRA 2, 3 MASAMBA 13-21
Ukwati ndiponso kukhala wosakwatira kapena wosakwatiwa ndi mphatso zochokera kwa Mulungu. Mphatso zonsezi ndi zabwino. Kaya tili m’banja kapena ayi, nkhanizi zifotokoza zifukwa zotithandiza kuyamikira mphatsozi ndiponso mmene tingasonyezere kuyamikira.
NKHANI ZOPHUNZIRA 4, 5 MASAMBA 22-30
Timafuna thandizo la Yehova kuti tikwaniritse kudzipereka kwathu kwa iye. Nkhanizi zifotokoza mmene mzimu woyera umatithandizira kulimbana ndi mayesero ndiponso zinthu zofooketsa, kupirira chizunzo ndi mavuto komanso kupewa kumangotengera zochita za anzathu.
M’MAGAZINI INO MULINSO NKHANI IZI:
7 Dzina la Mulungu M’chigwa cha ku Switzerland
9 Ndimayamikira Kutumikira Yehova, Ngakhale pa Nthawi Zovuta
31 Muziganizira Zimene Yehova Wakuchitirani Kale
[Mawu a Chithunzi patsamba 2]
© Stähli Rolf A/age fotostock