Zamkatimu
February 15, 2012
© 2012 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania. Ulamuliro wonse pa magazini ino n’ngwathu.
Magazini Yophunzira
NKHANI ZOPHUNZIRA
APRIL 2-8, 2012
Tsanzirani Yesu pa Nkhani Yokhala Maso
TSAMBA 3 • NYIMBO: 108, 74
APRIL 9-15, 2012
‘Khalani Olimba Mtima Kwambiri Ndipo Muchite Zinthu Mwamphamvu’
TSAMBA 10 • NYIMBO: 101, 92
APRIL 16-22, 2012
Thandizani Mpingo Kukhalabe ndi Maganizo Abwino
TSAMBA 18 • NYIMBO: 20, 75
APRIL 23-29, 2012
N’zotheka Kukhala Osangalala M’banja Limene Wina Si Mboni
TSAMBA 26 • NYIMBO: 76, 56
CHOLINGA CHA NKHANI ZOPHUNZIRA
NKHANI YOPHUNZIRA 1 TSAMBA 3-7
N’chifukwa chiyani Yesu analimbikitsa otsatira ake kukhalabe maso? Nkhaniyi ikusonyeza mmene Khristu anasonyezera kuti anali maso padziko lapansi. Tiona njira zitatu zimene anasonyezera zimenezi komanso mmene tingamutsanzirire.
NKHANI YOPHUNZIRA 2 TSAMBA 10-14
Kodi tingapindule chilichonse poona mmene atumiki a Yehova otchulidwa m’Baibulo anasonyezera kulimba mtima? Nkhani ino iyankha funso limeneli ndipo itithandiza kuti nafenso tizichita zinthu molimba mtima.
NKHANI YOPHUNZIRA 3 TSAMBA 18-22
Munthu aliyense amakhala ndi khalidwe linalake lapadera. Nkhani ino itithandiza kuona mmene tingathandizire mpingo kukhala ndi maganizo abwino.
NKHANI YOPHUNZIRA 4 TSAMBA 26-30
Ngati munthu wina m’banja si mboni, Mkhristu amakumana ndi mayesero. Nkhani ino ikufotokoza zimene Akhristu amene ali m’mabanja oterewa angachite kuti m’banja mwawo mukhale mtendere komanso kuti athandize enawo kuphunzira choonadi.
M’MAGAZINI INO MULINSO NKHANI IZI
8 Ankalalikira Mawu a Mulungu Molimba Mtima
15 Kaduka ndi Khalidwe Limene Lingawononge Maganizo Athu
23 Natani Anali Wokhulupirika Ndipo Ankalimbikitsa Kulambira Koona
31 Kale Lathu
PATSAMBA LOYAMBA: Pa malo okwerera sitima ku New Delhi, m’dziko laIndia. Tsiku lililonse pamabwera masitima oposa 300. Abale amalalikira kwa anthu amene amabwera kudzagwira ntchito ndiponso kwa anthu apaulendo ochokera m’madera osiyanasiyana m’dzikoli
INDIA
KULI ANTHU OKWANA
1,224,614,000
KULI OFALITSA OKWANA
33,182
OFALITSA AWONJEZEKA NDI
5 peresenti