Zamkatimu
March 1, 2012
© 2012 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania. Ulamuliro wonse pa magazini ino n’ngwathu.
Kodi Mungawadziwe Bwanji Akhristu Oona?
NKHANI ZOYAMBIRIRA
3 Kodi Anthu Onse Omwe Amati Ndi Akhristu Ndi Akhristudi?
4 ‘Muzisunga Mawu Anga Nthawi Zonse’
7 ‘Ine Ndachititsa Kuti Adziwe Dzina Lanu’
8 “Uthenga Wabwino Uwu wa Ufumu Udzalalikidwa”
NKHANI ZA NTHAWI ZONSE
16 Phunzirani Zimene Mawu a Mulungu Amanena—Kodi Tizikumbukira Bwanji Imfa ya Yesu?
19 Yandikirani Mulungu—“Zinthu Zakale Sizidzakumbukiridwanso”
23 Zimene Owerenga Amafunsa—Kodi Chiphunzitso cha Utatu N’chochokera M’Baibulo?
30 Phunzitsani Ana Anu—“Anapitiriza Kumamatira Yehova”
M’MAGAZINI INO MULINSO NKHANI IZI:
10 Kodi Ndi Bwino Kuweruza Munthu Potengera Maonekedwe Ake?
13 Aaziteki Ayamba Kuphunzira Choonadi
20 Kodi N’kulakwa Kukhulupirira Zamizimu?