Zamkatimu
July July 15, 2012
© 2012 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania. Ulamuliro wonse pa magazini ino n’ngwathu.
Magazini Yophunzira
NKHANI ZOPHUNZIRA
AUGUST 27, 2012–SEPTEMBER 2, 2012
Lolani Yehova Kukutsogolerani ku Ufulu Weniweni
TSAMBA 7 • NYIMBO: 107, 27
SEPTEMBER 3-9, 2012
Tumikirani Mulungu Amene Amapereka Ufulu
TSAMBA 12 • NYIMBO: 120, 129
SEPTEMBER 10-16, 2012
“Ndingachitenso Mantha ndi Ndani?”
TSAMBA 22 • NYIMBO: 33, 45
SEPTEMBER 17-23, 2012
Yehova Akusonkhanitsa Banja Lake
TSAMBA 27 • NYIMBO: 53, 124
CHOLINGA CHA NKHANI ZOPHUNZIRA
NKHANI ZOPHUNZIRA 1, 2 TSAMBA 7-16
Yehova amafuna kuti atumiki ake onse akhale ndi ufulu wambiri. M’nkhani zimenezi, muona kuti iye akutiphunzitsa kukhala ndi ufulu. Tionanso zimene Satana akuchita kuti atiphere ufuluwo potichititsa kuganiza kuti dzikoli likhoza kutipatsa ufulu.
NKHANI YOPHUNZIRA 3 TSAMBA 22-26
N’chifukwa chiyani tikupitiriza kulalikira mwakhama ngakhale kuti anthu amatitsutsa komanso mavuto azachuma akuchuluka? Zifukwa zake zili mu Salimo 27 ndipo nkhaniyi yachokera m’lemba limeneli.
NKHANI YOPHUNZIRA 4 TSAMBA 27-31
Dongosolo la Mulungu, lomwe Paulo anatchula m’kalata yake yopita kwa Aefeso, likugwira ntchito masiku ano. Nkhaniyi ifotokoza mbali zina za m’kalatayi ndipo itithandiza kumvetsa cholinga cha dongosolo limeneli. Itithandizanso kuchita zinthu mogwirizana nalo.
M’MAGAZINI INO MULINSO NKHANI IZI
3 Anadzipereka ndi Mtima Wonse ku Ecuador
17 Yehova Anandiphunzitsa Kuchita Chifuniro Chake
32 “Zimene Ndinkafuna Zatheka”
PATSAMBA LOYAMBA: Akulalikira m’chinenero chamanja m’mzinda wa Rio de Janeiro ku Comunidade da Rocinha
M’GAWO LA CHINENERO CHAMANJA KU BRAZIL
MULI MIPINGO
358
MULI TIMAGULU
460
MULI MADERA
18