Zamkatimu
September 15, 2012
© 2012 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania. Ulamuliro wonse pa magazini ino ndi wathu.
Magazini Yophunzira
NKHANI ZOPHUNZIRA
OCTOBER 22-28, 2012
TSAMBA 3 • NYIMBO: 133, 132
OCTOBER 29, 2012–NOVEMBER 4, 2012
Mtendere Udzayamba mu Ulamuliro wa Zaka 1,000
TSAMBA 8 • NYIMBO: 55, 134
NOVEMBER 5-11, 2012
Tsanzirani Kuleza Mtima kwa Yehova ndi Yesu
TSAMBA 18 • NYIMBO: 35, 90
NOVEMBER 12-18, 2012
“Simukudziwa Tsiku Kapena Ola Lake”
TSAMBA 23 • NYIMBO: 43, 92
NOVEMBER 19-25, 2012
Yehova Amasonkhanitsa Anthu Ake Osangalala
TSAMBA 28 • NYIMBO: 119, 118
CHOLINGA CHA NKHANI ZOPHUNZIRA
NKHANI ZOPHUNZIRA 1, 2 TSAMBA 3-12
Pali zinthu zikuluzikulu zimene zichitike posachedwapa. Nkhanizi zikufotokoza zinthu 10 zimene zichitike. Zinthu zisanu ndi zokhudza kuwononga dziko la Satanali ndipo zinazo ndi zokhudza kukhazikitsa dziko latsopano.
NKHANI YOPHUNZIRA 3 TSAMBA 18-22
Tonsefe timayembekezera nthawi imene zinthu zoipa zidzathe ndipo dzikoli lidzakhala Paradaiso. Kaya mwakhala mukuyembekezera kwa miyezi yochepa kapena zaka zambiri, kuleza mtima n’kofunika. Nkhaniyi ikufotokoza zimene zingatithandize kukhala oleza mtima kwambiri.
NKHANI YOPHUNZIRA 4 TSAMBA 23-27
Anthu onse a Mulungu akufuna kuti dziko loipali lithe basi. Nkhaniyi ikusonyeza kuti kusadziwa tsiku kapena ola la mapeto kuli ndi ubwino wake.
NKHANI YOPHUNZIRA 5 TSAMBA 28-32
Kuyambira kale, misonkhano ikuluikulu yakhala yofunika kwambiri kwa anthu a Mulungu. Nkhaniyi ikufotokoza misonkhano yosaiwalika yotchulidwa m’Baibulo ndiponso ya masiku ano. Ikufotokozanso ubwino wa kupezeka pa misonkhanoyi.
M’MAGAZINI INO MULINSO NKHANI IYI
13 Sukulu Zophunzitsa Atumiki a Mulungu Zimasonyeza Kuti Yehova Amatikonda
PATSAMBA LOYAMBA: Abale ku Philippines amayesetsa kulalikira kwa anthu onse. Apa akulalikira kwa munthu yemwe ali pa njinga yokhala ndi kangolo ndipo ali kumpoto kwa chilumba cha Luzon
PHILIPPINES
KULI OFALITSA
177,635
APAINIYA OKHAZIKIKA
29,699
OBATIZIDWA MU 2011
8,586
AMAMASULIRA MABUKU M’ZINENERO
21