Zamkatimu
October 15, 2012
© 2012 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania. Ulamuliro wonse pa magazini ino n’ngwathu.
Magazini Yophunzira
NKHANI ZOPHUNZIRA
NOVEMBER 26, 2012–DECEMBER 2, 2012
Limbani Mtima Pokumana ndi Mavuto
TSAMBA 7 • NYIMBO: 81, 33
DECEMBER 3-9, 2012
TSAMBA 12 • NYIMBO: 122, 124
DECEMBER 10-16, 2012
Mverani Mulungu Kuti Mupindule ndi Malumbiro Ake
TSAMBA 22 • NYIMBO: 129, 95
DECEMBER 17-23, 2012
TSAMBA 27 • NYIMBO: 63, 125
CHOLINGA CHA NKHANI ZOPHUNZIRA
NKHANI YOPHUNZIRA 1 TSAMBA 7-11
Masiku ano, mavuto ndi osachita kunena. Nkhaniyi itithandiza kuona zimene tikuphunzira kwa anthu akale ndiponso a masiku ano amene analimba mtima pokumana ndi mavuto aakulu. Ikufotokozanso zimene zingatithandize kukhala olimba mtima kwambiri ndiponso osangalala zivute zitani.
NKHANI YOPHUNZIRA 2 TSAMBA 12-16
Masiku ano, anthu salimbikitsana, m’malomwake amangokhumudwitsana. M’nkhani ino tiona zinthu zosokoneza mtendere mu mpingo zimene tiyenera kupewa. Tikambirananso zimene tingachite kuti tizigwirizana ndi anzathu.
NKHANI YOPHUNZIRA 3, 4 TSAMBA 22-31
Nkhani yoyamba ikusonyeza kuti Mulungu walumbira kuti akwaniritsa malonjezo ake. Kuti tidzapindule ndi malonjezowa, tiyenera kumvera Mulungu komanso kuchita zimene talonjeza. Nkhani yachiwiri ikufotokoza za anthu amene anachitadi zimene analonjeza. Ikulimbikitsa Akhristu onse obatizidwa kuti akwaniritse “Inde” wawo wofunika kwambiri.—Mat. 5:37.
M’MAGAZINI INO MULINSO NKHANI IZI
3 Anadzipereka ndi Mtima Wonse ku Brazil
17 Ubwenzi wa Zaka 60, Koma Akuti N’chiyambi Chabe
32 Mawu Olimbikitsa a “Ana Aang’ono”
PATSAMBA LOYAMBA: Banja limene likuchita upainiya, likulalikira kumbali ya mzinda kumene kumadutsa anthu ambiri. Likugwiritsa ntchito shelefu ya matayala
DERA LA TIMES SQUARE KU MANHATTAN, KU NEW YORK CITY
APAINIYA
600
AMALALIKIRA KU MANHATTAN M’MADERA
12
KULI MIPINGO
55