Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • w13 3/15 tsamba 1-2
  • Zamkatimu

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Zamkatimu
  • Nsanja ya Olonda—2013
  • Timitu
  • MAGAZINI YOPHUNZIRA
  • NKHANI ZOPHUNZIRA
  • M’MAGAZINI INO MULINSO NKHANI IZI
Nsanja ya Olonda—2013
w13 3/15 tsamba 1-2

Zamkatimu

March 15, 2013

© 2013 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania. Ulamuliro wonse pa magazini ino n’ngwathu.

MAGAZINI YOPHUNZIRA

APRIL 29, 2013–MAY 5, 2013

Anthu Okonda Yehova ‘Alibe Chowakhumudwitsa’

TSAMBA 3 • NYIMBO: 45, 32

MAY 6-12, 2013

Kodi Muli ndi “Mtima Wodziwa” Yehova?

TSAMBA 8 • NYIMBO: 62, 60

MAY 13-19, 2013

Popeza “Mwadziwa Mulungu,” Kodi Muyenera Kuchita Chiyani?

TSAMBA 13 • NYIMBO: 81, 135

MAY 20-26, 2013

Yehova Ndi Malo Athu Okhalamo

TSAMBA 19 • NYIMBO: 51, 95

MAY 27, 2013–JUNE 2, 2013

Muzilemekeza Dzina Lalikulu la Yehova

TSAMBA 24 • NYIMBO: 27, 101

NKHANI ZOPHUNZIRA

▪ Anthu Okonda Yehova ‘Alibe Chowakhumudwitsa’

Akhristu onse ali pa mpikisano wokalandira mphoto ya moyo wosatha. Koma popeza ndife opanda ungwiro, timapunthwa. M’nkhaniyi tikambirana zinthu zisanu zimene zingatipunthwitse. Ifotokozanso mmene tingapewere zinthu zimenezi kuti tipambane mpikisanowu.

▪ Kodi Muli ndi “Mtima Wodziwa” Yehova?

Buku la Yeremiya limatiuza zambiri pa nkhani ya mtima wophiphiritsa. Nkhaniyi itithandiza kudziwa ‘mtima wosadulidwa’ komanso kuopsa kokhala ndi mtima wotero ngakhale kwa Akhristu. Itithandizanso kudziwa zimene tingachite kuti tikhale ndi “mtima wodziwa” Yehova.—Yer. 9:26; 24:7.

▪ Popeza “Mwadziwa Mulungu,” Kodi Muyenera Kuchita Chiyani?

Kodi munthu amachita zinthu ziti kuti adziwe Mulungu komanso kuti adziwidwe ndi Mulunguyo? N’chifukwa chiyani munthu afunika kukulabe ngakhale atakhala m’choonadi kwa zaka zambiri ndipo angachite bwanji zimenezi? Nkhaniyi iyankha mafunso amenewa.

▪ Yehova Ndi Malo Athu Okhalamo

Ngakhale kuti tikukhala m’dziko loipa sitiyenera kuchita mantha. Nkhaniyi ikusonyeza kuti Yehova Mulungu amateteza anthu ake nthawi zonse.

▪ Muzilemekeza Dzina Lalikulu la Yehova

Kodi kudziwika ndi dzina la Mulungu kumatanthauza chiyani? Nanga kuyenda m’dzinali kumatanthauza chiyani? Kodi Mulungu amaona bwanji anthu amene amanyoza dzina lake? Nkhaniyi ili ndi mayankho a mafunso amenewa.

M’MAGAZINI INO MULINSO NKHANI IZI

18 Tizitonthozana

29 Kodi Josephus Analembadi Zimenezi?

30 Musataye Mtima

PATSAMBA LOYAMBA: Dziko la Finland lili m’mphepete mwa nyanja ndipo lili ndi zilumba zambiri. Kulinso nyanja zambiri makamaka kudera la pakati ndiponso kum’mawa kwa dzikoli. Ofalitsa akamapita kukalalikira kumadera amene kulibe ofalitsa ambiri amayenda pa boti

FINLAND

KULI ANTHU:

5,375,276

WOFALITSA ALIYENSE AYENERA KULALIKIRA ANTHU:

283

KULI APAINIYA OKHAZIKIKA:

1,824

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena