Zamkatimu
April 15, 2013
© 2013 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania. Ulamuliro wonse pa magazini ino n’ngwathu.
MAGAZINI YOPHUNZIRA
JUNE 3-9, 2013
Zimene Mungachite Kuti Muzipindula Powerenga Baibulo
TSAMBA 7 • NYIMBO: 114, 113
JUNE 10-16, 2013
Mawu a Mulungu Azikuthandizani Ndipo Muzithandiza Nawo Ena
TSAMBA 12 • NYIMBO: 37, 92
JUNE 17-23, 2013
“Muzitsimikizira Kuti Zinthu Zofunika Kwambiri Ndi Ziti”
TSAMBA 22 • NYIMBO: 70, 98
JUNE 24-30, 2013
TSAMBA 27 • NYIMBO: 129, 63
NKHANI ZOPHUNZIRA
▪ Zimene Mungachite Kuti Muzipindula Powerenga Baibulo
▪ Mawu a Mulungu Azikuthandizani Ndipo Muzithandiza Nawo Ena
Paulo analemba kuti: “Mawu a Mulungu ndi amoyo ndi amphamvu.” (Aheb. 4:12) Koma mphamvuyi ikhoza kutithandiza ngati timaphunzira Mawuwo ndiponso kutsatira zimene timaphunzirazo. Nkhanizi zikufotokoza zimene tingachite kuti tizipindula pophunzira Baibulo. Zikufotokozanso zimene tingachite kuti nzeru yochokera kwa Mulungu izititsogolera pa moyo wathu komanso mu utumiki.
▪ “Muzitsimikizira Kuti Zinthu Zofunika Kwambiri Ndi Ziti”
▪ Musatope Kuchita Zabwino
Ndi mwayi waukulu kukhala m’gulu la Mulungu lomwe lili ndi mbali ina padziko lapansi, ina kumwamba. Kodi tingathandize bwanji kuti ntchito ya gululi iziyenda bwino? Nanga n’chiyani chingatithandize kuti tizichita zinthu mogwirizana ndi gulu la Yehova komanso kuti tisatope? Nkhanizi ziyankha mafunso amenewa.
M’MAGAZINI INO MULINSO NKHANI IZI
3 Anadzipereka ndi Mtima Wonse ku Mexico
17 Tachita Utumiki wa Nthawi Zonse kwa Zaka 50 Kumpoto Kwenikweni
PATSAMBA LOYAMBA: M’mipingo yambiri, abale amakumana 7:30 m’mawa kapena kum’mawa kwambiri kuti akalalikire. Iwo amayesetsa kulalikira kwa anthu amene amakumana nawo mumsewu
NEPAL
KULI ANTHU
26,620,809
KULI OFALITSA
1,667
AMACHITITSA MAPHUNZIRO A BAIBULO
3,265