Zamkatimu
July 15, 2013
© 2013 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania. Ulamuliro wonse pa magazini ino n’ngwathu.
MAGAZINI YOPHUNZIRA
SEPTEMBER 2-8, 2013
“Tiuzeni, Kodi Zinthu Zimenezi Zidzachitika Liti?”
TSAMBA 3 • NYIMBO: 128, 101
SEPTEMBER 9-15, 2013
“Dziwani Kuti Ine Ndili Pamodzi ndi Inu Masiku Onse”
TSAMBA 9 • NYIMBO: 30, 109
SEPTEMBER 16-22, 2013
Yesu Amadyetsa Anthu Ambiri Kudzera mwa Anthu Ochepa
TSAMBA 15 • NYIMBO: 108, 117
SEPTEMBER 23-29, 2013
“Ndani Kwenikweni Amene Ali Kapolo Wokhulupirika ndi Wanzeru?”
TSAMBA 20 • NYIMBO: 107, 116
NKHANI ZOPHUNZIRA
▪ “Tiuzeni, Kodi Zinthu Zimenezi Zidzachitika Liti?”
▪ “Dziwani Kuti Ine Ndili Pamodzi ndi Inu Masiku Onse”
Nkhani zimenezi zikufotokoza mavesi ena a Mateyu chaputala 24 ndi 25. Zikusintha zinthu zina zimene tinkakhulupirira zokhudza nthawi imene ulosi wa Yesu wonena za masiku otsiriza ndiponso wokhudza tirigu ndi namsongole, uyenera kukwaniritsidwa. Nkhanizi zikufotokozanso mmene kusintha kumeneku kungatithandizire.
▪ Yesu Amadyetsa Anthu Ambiri Kudzera mwa Anthu Ochepa
▪ “Ndani Kwenikweni Amene Ali Kapolo Wokhulupirika ndi Wanzeru?”
Yesu ankadyetsa anthu ambiri kudzera mwa anthu ochepa. Ankachita zimenezi podyetsa khamu la anthu mozizwitsa komanso popereka chakudya chauzimu kwa otsatira ake. Nkhani yoyamba ikufotokoza za anthu ochepa amene ankawagwiritsa ntchito podyetsa Akhristu oyambirira. Nkhani yachiwiri ikufotokoza za anthu ochepa amene Khristu akuwagwiritsa ntchito potidyetsa masiku ano.
M’MAGAZINI INO MULINSO NKHANI IZI
26 M’bale Watsopano M’Bungwe Lolamulira
PATSAMBA LOYAMBA: Akulalikira kunyumba ndi nyumba ku Bukimba, m’dera la Runda m’dziko la Rwanda
RWANDA
Wa Mboni mmodzi pa anayi alionse m’dzikoli akuchita upainiya. A Mboni ena onse akhama amalalikira maola pafupifupi 20 mwezi uliwonse.
MBONI
22,734
MAPHUNZIRO A BAIBULO
52,123
OPEZEKA PA CHIKUMBUTSO MU 2012
69,582