Zamkatimu
August 15, 2013
© 2013 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania. Ulamuliro wonse pa magazini ino n’ngwathu.
MAGAZINI YOPHUNZIRA
SEPTEMBER 30, 2013–OCTOBER 6, 2013
TSAMBA 3 • NYIMBO: 125, 66
OCTOBER 7-13, 2013
TSAMBA 10 • NYIMBO: 119, 80
OCTOBER 14-20, 2013
Tiziganizirana Ndiponso Kulimbikitsana
TSAMBA 18 • NYIMBO: 124, 20
OCTOBER 21-27, 2013
Ganizirani za Mtundu wa Munthu Amene Muyenera Kukhala
TSAMBA 23 • NYIMBO: 61, 43
NKHANI ZOPHUNZIRA
▪ Mwapatulidwa
Atumiki a Yehovafe tapatulidwa kuti tizitumikira Mulungu. M’nkhaniyi tikambirana Nehemiya chaputala 13. Tiona zinthu 4 zimene zingatithandize kuti tikhalebe oyera.
▪ ‘Musakwiyire Yehova’
Nkhaniyi ikufotokoza zinthu 5 zimene zingachititse Mkhristu wokhulupirika kuyamba ‘kukwiyira Yehova.’ (Miy. 19:3) Ikufotokozanso zinthu 5 zimene zingatithandize kuti tisayambe n’komwe kuimba Yehova mlandu pa mavuto athu.
▪ Tiziganizirana Ndiponso Kulimbikitsana
▪ Ganizirani za Mtundu wa Munthu Amene Muyenera Kukhala
Nkhani yoyamba ikufotokoza zimene tingachite kuti tithandizane kukhalabe okhulupirika ngakhale kuti tikukumana ndi mavuto. Yachiwiri ikusonyeza zimene tingachite kuti Satana asasokoneze ubwenzi wathu ndi Mulungu.
M’MAGAZINI INO MULINSO NKHANI IZI
8 Mafunso Ochokera kwa Owerenga
9 Yehova ‘Amanyamula Katundu Wanga Tsiku ndi Tsiku’
15 Makolo, Phunzitsani Ana Anu Kuyambira Ali Akhanda
28 Elisa Anaona Magaleta Oyaka Moto, Kodi Inunso Mukuwaona?
31 Kale Lathu
PATSAMBA LOYAMBA: Akulalikira kunyumba ndi nyumba m’mudzi wa Erap. Uwu ndi umodzi mwa midzi ya m’chigwa ku Morobe m’dziko la Papua New Guinea
PAPUA NEW GUINEA
Kuli Anthu: 7,013,829
Kuli Ofalitsa: 3,770
Apainiya Okhazikika: 367
Maphunziro a Baibulo: 5,091
Opezeka pa Chikumbutso mu 2012: 28,909
Amamasulira mabuku: M’zinenero 14
Zinali ngati wofalitsa aliyense analandira alendo 6 pa Chikumbutso