Zamkatimu
September 15, 2013
© 2013 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania. Ulamuliro wonse pa magazini ino n’ngwathu.
MAGAZINI YOPHUNZIRA
OCTOBER 28, 2013–NOVEMBER 3, 2013
Zikumbutso za Yehova Ndi Zodalirika
TSAMBA 7 • NYIMBO: 64, 114
NOVEMBER 4-10, 2013
Kodi Zikumbutso za Yehova Zimakondweretsa Mtima Wanu?
TSAMBA 12 • NYIMBO: 116, 52
NOVEMBER 11-17, 2013
TSAMBA 17 • NYIMBO: 69, 106
NOVEMBER 18-24, 2013
TSAMBA 22 • NYIMBO: 27, 83
NOVEMBER 25, 2013–DECEMBER 1, 2013
Upainiya Umalimbitsa Ubwenzi Wathu ndi Mulungu
TSAMBA 27 • NYIMBO: 95, 104
NKHANI ZOPHUNZIRA
▪ Zikumbutso za Yehova Ndi Zodalirika
▪ Kodi Zikumbutso za Yehova Zimakondweretsa Mtima Wanu?
Yehova wakhala akugwiritsa ntchito zikumbutso zake potsogolera anthu ake. Kodi zikumbutso zakezo n’chiyani? Nkhani yoyamba ikufotokoza chifukwa chake tiyenera kukhulupirira zikumbutso za Mulungu. Yachiwiri ikufotokoza zinthu zitatu zimene zingatithandize kukhulupirira kwambiri zikumbutso za Yehova.
▪ Kodi Mwasandulika?
▪ Muzisankha Zochita Mwanzeru
Anthufe timachita zinthu mogwirizana ndi mmene tinakulira ndi kumene timakhala. Kodi tingatani kuti tizisankha zochita mogwirizana ndi zimene Mulungu amafuna? Nanga n’chiyani chingatithandize kuti tichitedi zimene tasankha? Nkhani ziwirizi zitithandiza kudzifufuza bwinobwino pa nkhaniyi.
▪ Upainiya Umalimbitsa Ubwenzi Wathu ndi Mulungu
M’nkhaniyi tiona zinthu 8 zimene zingatithandize kulimbitsa ubwenzi wathu ndi Yehova tikamachita upainiya. Ngati panopa mukuchita upainiya, kodi n’chiyani chingakuthandizeni kupitiriza ngakhale mutakumana ndi mavuto? Nanga mungatani ngati mukufuna kuchita upainiya ndi kulandira madalitso ake?
M’MAGAZINI INO MULINSO NKHANI IZI
PATSAMBA LOYAMBA: Abale ndi alongo a kudera la Amazonas, kumpoto kwa dziko la Peru, amagwiritsa ntchito mpata uliwonse kuti alalikire
PERU
KULI ANTHU OKWANA
29,734,000
KULI OFALITSA OKWANA
117,245
ANTHU AMENE ABATIZIDWA PA ZAKA 5 ZAPITAZI
28,824
M’dziko la Peru, amamasulira mabuku athu m’zinenero 6. Kuli apainiya apadera ndiponso amishonale oposa 120 amene amalalikira m’zinenero zina osati Chisipanishi chokha