Zamkatimu
February 15, 2014
© 2014 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania.
NKHANI ZOPHUNZIRA
APRIL 7-13, 2014
Tamandani Khristu, Mfumu Yaulemerero
TSAMBA 3 • NYIMBO: 99, 107
APRIL 14-20, 2014
Sangalalani Chifukwa cha Ukwati wa Mwanawankhosa
TSAMBA 8 • NYIMBO: 109, 100
APRIL 21-27, 2014
Yehova Amatipatsa Zinthu Zofunika Ndipo Amatiteteza
TSAMBA 16 • NYIMBO: 60, 51
APRIL 28, 2014–MAY 4, 2014
TSAMBA 21 • NYIMBO: 91, 63
NKHANI ZOPHUNZIRA
▪ Tamandani Khristu, Mfumu Yaulemerero
▪ Sangalalani Chifukwa cha Ukwati wa Mwanawankhosa
Yesu Khristu, yemwe ndi Mfumu, anamangirira lupanga lake n’kukwera pahatchi kuti akagonjetse adani ake. Akamaliza kuwagonjetsa adzakwatira mkazi wokongola woperekezedwa ndi anamwali anzake. Nkhani yosangalatsayi yafotokozedwa mu Salimo 45. Werengani kuti muone mmene nkhaniyi ikukukhudzirani.
▪ Yehova Amatipatsa Zinthu Zofunika Ndipo Amatiteteza
▪ Yehova Ndi Mnzathu Weniweni
N’chiyani chingatithandize kuti tiziona kuti Yehova ndi Atate wathu wakumwamba? Nkhanizi zitithandiza kuti tizigwirizana kwambiri ndi Yehova, yemwe amatipatsa zofunika, amatiteteza komanso ndi Mnzathu weniweni. Zitilimbikitsanso kuti tizithandiza ena kuti ayambe kumulemekeza.
M’MAGAZINIYI MULINSO NKHANI IZI
13 Mkazi Wamasiye wa ku Zarefati Anadalitsidwa Chifukwa cha Chikhulupiriro
26 Mafunso Ochokera kwa Owerenga
30 Kale Lathu
PATSAMBA LOYAMBA: Pamalo awa (Michaelerplatz) mumzinda wa Vienna pamapezeka anthu ambiri ndipo ndi malo abwino kulalikirapo uthenga wa m’Baibulo. Mlongoyu akulalikira m’Chitchainizi ndipo akugawira buku lakuti, Kodi Baibulo Limaphunzitsa Chiyani Kwenikweni?
AUSTRIA
KULI OFALITSA OKWANA
20,923
APAINIYA
2,201
MAPHUNZIRO A BAIBULO
10,987
Mumzindawu uthenga wabwino wa Ufumu umalalikidwa m’zinenero 25