Zamkatimu
April 15, 2014
© 2014 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
MAGAZINI YOPHUNZIRA
JUNE 2-8, 2014
Tsanzirani Chikhulupiriro cha Mose
TSAMBA 3 • NYIMBO: 33, 133
JUNE 9-15, 2014
TSAMBA 8 • NYIMBO: 81, 132
JUNE 16-22, 2014
TSAMBA 17 • NYIMBO: 62, 106
JUNE 23-29, 2014
Limbani Mtima, Yehova Akuthandizani
TSAMBA 22 • NYIMBO: 22, 95
JUNE 30, 2014–JULY 6, 2014
Yehova Amaona Mavuto Athu N’kutithandiza
TSAMBA 27 • NYIMBO: 69, 120
NKHANI ZOPHUNZIRA
▪ Tsanzirani Chikhulupiriro cha Mose
▪ Kodi ‘Mukuona Wosaonekayo’?
Mwa chikhulupiriro, Mose ankatha kuona zinthu zosaoneka. Nkhani ziwirizi zikufotokoza mmene ifeyo tingasonyezere chikhulupiriro ngati Mose n’kupitiriza “kupirira moleza mtima ngati kuti tikuona Wosaonekayo.”—Aheb. 11:27.
▪ Simungatumikire Ambuye Awiri
▪ Limbani Mtima, Yehova Akuthandizani
Anthu ambirimbiri padziko lonse akupita m’mayiko ena kukafuna ntchito. Ambiri amasiya amuna kapena akazi awo komanso ana. Nkhanizi zitithandiza kumvetsa zimene Yehova akufuna kuti tizichita pokwaniritsa udindo wathu wosamalira banja komanso mmene amatithandizira kuti tikwaniritse udindo umenewu.
▪ Yehova Amaona Mavuto Athu N’kutithandiza
Tikamawerenga mawu akuti “maso a Yehova ali paliponse,” ena amaganiza kuti Mulungu amatiyang’anitsitsa kuti aone zimene tikulakwitsa n’kutilanga. Zimenezi zimachititsa kuti asamafune kumutumikira. (Miy. 15:3) Koma nkhaniyi itithandiza kuona njira 5 zosonyeza mmene timapindulira, Yehova akamatiyang’ana.
M’MAGAZINIYI MULINSO NKHANI IZI
PATSAMBA LOYAMBA: M’bale akulalikira kwa munthu amene akumumeta tsitsi ku Istanbul, ndipo akum’patsa kabuku kakuti Uthenga Wabwino
TURKEY
KULI ANTHU OKWANA
75,627,384
KULI OFALITSA OKWANA
2,312
MAPHUNZIRO A BAIBULO
1,632
WOFALITSA ALIYENSE
Ayenera kulalikira anthu 32,711
Kuchokera mu 2004 chiwerengero cha apainiya okhazikika ku Turkey chawonjezeka ndi 165%