Zamkatimu
May 15, 2014
© 2014 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
MAGAZINI YOPHUNZIRA
JULY 7-13, 2014
Kodi ‘Tingayankhe Bwanji Wina Aliyense’?
TSAMBA 6 • NYIMBO: 96, 93
JULY 14-20, 2014
Muzichitira Anthu Zimene Mungafune Kuti Akuchitireni
TSAMBA 11 • NYIMBO: 73, 98
JULY 21-27, 2014
Yehova Ndi Mulungu Wadongosolo
TSAMBA 21 • NYIMBO: 125, 53
JULY 28, 2014–AUGUST 3, 2014
Kodi Mukuyenda Limodzi ndi Gulu la Yehova?
TSAMBA 26 • NYIMBO: 45, 27
NKHANI ZOPHUNZIRA
▪ Kodi ‘Tingayankhe Bwanji Wina Aliyense’?
▪ Muzichitira Anthu Zimene Mungafune Kuti Akuchitireni
Nthawi zina anthu amatifunsa mafunso ovuta mu utumiki. Nkhani yoyamba itithandiza kudziwa zinthu zitatu zimene tingachite kuti tiziwayankha mogwira mtima. (Akol. 4:6) Nkhani yachiwiri ikusonyeza kufunika kotsatira mawu a Yesu a pa Mateyu 7:12 tikamalalikira.
▪ Yehova Ndi Mulungu Wadongosolo
▪ Kodi Mukuyenda Limodzi ndi Gulu la Yehova?
Yehova wakhala akuthandiza atumiki ake kuchita zinthu mwadongosolo. Nkhani ziwirizi zikusonyeza zimene Mulungu amafuna kuti tizichita. Ikusonyezanso chifukwa chake tiyenera kuyenda limodzi ndi gulu la Yehova masiku ano.
M’MAGAZINIYI MULINSO NKHANI IZI
3 ‘Chakudya Changa N’kuchita Chifuniro cha Mulungu’
16 Yehova Wandithandiza Kwambiri
31 Kale Lathu
PATSAMBA LOYAMBA: Akulalikira kumsika wa nsomba. Anthu a pachilumbachi amalankhula zilankhulo zoposa 20
SAIPAN
KULI ANTHU
48,220
KULI OFALITSA
201
KULI APAINIYA OKHAZIKIKA
32
KULI APAINIYA OTHANDIZA
76
Opezeka pa Chikumbutso mu 2013 analipo 570